Email a copy of 'CCAP controversies rages on: Livingstonia battle and Blantyre Synod infighting' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'CCAP controversies rages on: Livingstonia battle and Blantyre Synod infighting' to a friend
Economics Association of Malawi (Ecama) has accused Daily Times newspaper of sensationalising their headline when it reported that “Mutharika lied...
This second deputy session clerk by the name of Hezron Banda mentioned here is this guy alright upstairs. Gwaaa mutu uja ulibedi nzeru eti? He is only second deputy meaning to say that there is first session clerk. Why is first session clerk quiet? He knows what he is doing angofuna kudyako dollar malova achina Loadings Kalua kudya koopsya muzayankha amaliongo inuuu. Hezron please slow down akulekela wekha game Muhangoyo game igona yake posachedwa mbamba deeeee. As for Kanengo uyo Muhango anaku pepererani mtera mwatsizinilatu pepani its not your fault. Ena kuyambana ndi abale awo, azikazi awo just bcoz of… Read more »
Holy ghost fire on both sides,achuluka ndimadyela.Mwasiya Nkhoma Pano nokha nokha shame on you Livingstonia may the lord have mercy Izi siza Mulungu koma work of devil
Wasted synod
Kungowonekeratu kuti zadziko izi Mzimu Woyera palibepo ngakhale pang’ono. Nanga za Mulungu mpaka Toyi Toyi munamva kuti? Maudindo a pa dziko. Masiku omaliza kuphelerezera Maulosi.
Achewa nsanje Atumbuka amene mukulimbana nawowo ndi anthu ochepa komaso sanalamulileko dzikoli inu achewa munyananu CHIFUKWA ife Atumbuka timapanga zaife osati zanu zokubazo.Osamangopitiriza kuba kwanuko bwanji? Foesek mxiiiim!!!!!chonsecho chilichose nsanje chanucho ndifukwa chake mhangoyo akupikitsidwa pa kanengopo.iwe phwisi nalimata ndiwe ntchebe wapulika
Christians created their own god,who can not give them directions shame on all christians in Malawi.You pretend to be knowleagable yet ndinu mbuzi zenizeni kumangolimbana ana a Mdierekezi Lucifer inu.I hate all yhe missionaries who came to Malawi to teach us this dirty religion which they themselves never practised. For example Dr.David Livingston came with this stupid religion but his brother William Livingston and his son in law AL Bruce were torchin churches at Magomero.Silly Atumbuka nonse
That is the problem with the churches that have he rule for pastors to be paid by their members at the congregation he is saving. Have a centre pay point. All the money should be put in one bag then structure the pay for every paster from the centre bag. Now a Pastor who is saving in rural areas earns little money. When people go to visit the Pasor they only carry mtedza, maize or chicken. There is little that the pastors benefits like the urban pastors. Nevertheless, God’s work is needed every where. Even the rural people want the… Read more »
ccap again.aliyense akufuna ndalama.ntchito kudelerana basi,ngati ,mukulephera ku mpingo,m’manyumba chikhalidwe chonunkha. komanso kunyoza anthu ena nde bizinesi zawo ,ndikupemphapempha ngati masikini bwana,zitsiru.miiix uhule nde simungafunse.kakakakakakakaka
Church? Do these peope understand the meaning of the word Church? Does ‘church’ in any way mean a fighting groung or rich mining area. Do they think this is one way of preaching to bring more people to their church? Over my dead body, i cannot associate myself with these thugs always fighting.
Zochita za atumbuka ndichoncho. Zamanyi mkhosi. Anthu adzikonda mopanda manyazi awa. Akakhala pantchito amangolembana okhaokha irrespective of their qualifications. Pakakhala mwayi otumiza munthu kunja, amangotumizana okhaokha. Ku ministry of lands, mtumbuka wina is busy distributing title deeds kwa atumbuka okhaokhanso.ku Director of Buildings capital hill kuli Mr Bandura mtumbuka yemwe amangochita take action pa ma project akumpoto okhaokha. Panyapanu atumbuka koma musayese kuti ife sitikuwona khalidwe lanu lonyansali. Ife zimatiwawa.