Email a copy of 'Court orders mother to sweep in classes for concealing birth' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

27 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
nyavizwazwa
nyavizwazwa
8 years ago

Anthu opanda nzeru will always castigate each other, but the truth is whether mulomwe, mutumbuka muyao angakhale mtundu uliwonse ngati zinthu sizinayende mwadongosolo victim amakhala mayi. Koma mayiyu tsono anakaganiza kuti ngati azibambo angondipatsa ana nkumapita the best way ndizitetedze ndekha. Ntchimo limene wapangali lilingati la David ndi Uriya Mziti. kuchitachigololo ndi kupha Uriya mwini mkazi. but what we should learn is that sin is never concealed. Who can hide the wreath of God? no body. Mayiyo akalape poti Mulungu ngwachifundo akhululuka koma asazachimwenso.

Eliam k
Eliam k
9 years ago

Thats a fair sentence considering the responsibility she is having, my appeal to her is azilera

Noel
Noel
9 years ago

Comment #22, ana apatchire komanso oti anakanidwa ndi abambo awo, sindikudziwa ngati ku utumbukako anawo amakakhala kuchimuna. And its my fisrt tym to hear this. I believe there z noting conncted 2 chikamwini here (they are illigitimate children).

shadreck Kalombola
9 years ago

Musatinyozere chikhalidwe chathu please jst coment on this matter only inu atumbuka mumatiyamba dala mufuna tizikusalaniso.mkazi walakwisa kutaya mwana ompeza peza tchimo limeneli mulunga azaweluza Ndi KWA onse anatengapo gawo pa mimba ya mwana ameneyu

Joe ku Nkhwivi
9 years ago

Chilango chomwe Magestrate akanapereka ndikulamula kuti akatsekese mokakamizidwa chifukwa akuzunzitsa ana osalakwa. Ana seven azidya chiyani? Azingozunzika amenewo.

SHAME ON CHIKAMWINI
SHAME ON CHIKAMWINI
9 years ago

THIS SINS ARE DEEPLY ROOTED IN CHIKAMWINI TRADITIONS -FOOLISH TRADITION ANA NI AMUKAZI.ASK TUMBUKAS -ANA NI A MWAMUNA AND SUCH CASES AS THESE ARE SCARCE.JUST LOOK AT THE SURNAME OF THE MOTHER-ALICK??? ANTU WOTAYA MTUNDU NDI ANA OMWE. SHAME ON CHIKAMWINI

Mmasomwambuyanu
Mmasomwambuyanu
9 years ago

After delivery, thats wen wazindikira kuti ndi mphawi. Nthawi yomwe ankamugona anali wolemera. Life was lost, if i were the magistrate, i would still give her a custodial sentence. Alomwe ndi zigololo!!!! 7 children opanda bambo and yet she is still not satisfied. Kulera bwanji kodi simukudziwa ndi umbuli wanji kodi alomwe inu???

ALINY AMENEWA
9 years ago

aaaaa sanadziwe mkaziyo zotsatila za zimene ankapanga?Munthu wa ana Seven ameneyo,God help us 2know da rght thng

Piper
Piper
9 years ago

What about the innocent dead baby….is it going to be dead for only 5 months !!! This is pathetic you horrible little bastards !!! What did the baby do to deserve such a terrible death And the mother gets 5 months sweeping ??? You are as guilty as the mother !!!! Stupid !!!

ALINY AMENEWA
9 years ago

Achewa nawoso ngopusa bwanj,she is telling us dat wen she waz doin sex she couldn’t know its results? sakudziwa ndi njira zakulera zomwe, Vichewa kkkkkk

Read previous post:
Flames camp training pictorial: Malawi date Zambia, South Africa and Egypt in strength testing matches

Malawi national football team aka the Flames will play three international matches in preparation for the Cosafa Cup and 2017...

Close