Email a copy of 'DPP MP Kalindo accused of land grab in Malawi tea-growing Thyolo' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP MP Kalindo accused of land grab in Malawi tea-growing Thyolo' to a friend
A brawl has ensued between Mzuzu Police and a family in Lusangazi, Nkhata Bay – on the outskirts of Mzuzu...
Muluzapo ntchito Winiko akudya zimbabwe atathamangitsa azungu zinthu zidasokonekera mpaka pano. Tea is the third after Tobacco,sugar it is better to avoid these things ,please know that all land belongs to government not individuals ,that is why you can be moved at any time despite having stayed for over 500 years.
Kwa adzungu munthu wakhungu lathu la ku Africa sangakhale ndi malo ochuluka motero ndipo amalandila chipepeso pa milandu ngakhale ya dzaka 100 zapita and zimatheka. Dziko lopanda ID, anthu amangotenga kalikonse mene afunila like Chambo, Mbewu ndi zinthu zina zochuluka. Kodi ku England ungatenge maluwa kubwera nawo ku Africa kapena ungapedzeke ndi farm yayikulu ngati EPM? Lets support Hon. Kalindo ngati uli ndi mantha uzingowapempherera kuti zonse zichitike. Tisasapote ndalama zomwe tikuhongedwa nazo kuti chilungamo chife.
Point of correction. T/A Tomasi not Thomas. Dzinali ndi spell yake imeneyo si chiyankhulidwe
we need landreform here in MALAWI
You came in 1914 from Mozambique, got employment in tea estates and claim the land was your ancestors’ My foot! Go claim your ancestors’ land in Ulongwe Mozambique.
Kodi mmesa nose ndinu ma m.p a dpp? Nde mukukangana dziyani apa?
Zikungosonyezeratu kuti ka chipani kanuko kalibe mwambo.
I think kalindoyu anthu sakumumvetsa bwino,dzikolino makolo anthu analandidwa malo mwakhanza ndipo palibe analandilapo
ngati chipepeso,ndiye MR KALINDO sikuti akulakwayi anthu amenewa anayenela to be compesed, thyolo,mulanje,anthu anangowakunjika ngati timilu tausipa
malo wonse azungu anagawana
dziko silimachuluka koma anthu ndiamene tikuchulukana,alandile chipepeso basi
That’s absolutely madness and if the pple of thyolo and mulanje go ahead with such stupidty, we also the ppof mangochi and machinga will mobilize ourselfs chasing away all those who came from mulanje and thyolo in the namae of kuzigulira malo, they too grabbed the yao land. Mapiko
Ine Nkhani Za Alhomwe Zimandinyasa Kwabasi
Comrade Winiko doing it in the Comrade-Robert-Gabriel-Mugabe style. Is this the messiah people of Mulanje and Thyolo have been waiting for? Winiko yemweyo kuti wawawa!