Email a copy of 'FAM blows out Carlsberg allocation, justifies expenditure' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'FAM blows out Carlsberg allocation, justifies expenditure' to a friend
At times, we have to accept that even a competent workforce would struggle to present a credible ‘premise’ for developing...
Apatseni ndalamazo a frames kuti amalize magemu awili otsala nanga mpakana nkhani pa BBC akamaliza kusewera ndi Ethiopia Kafukuku ayambike ku FAM komanso tikufuna anthu a nyuwani ku Fam.
Anthu awa ndi akubadi asasewere mpira tione momwe zikhalire. kunjaku anthu akusowa thandizo la mankhwala koma ena mkumaseweretsa ndalama zambirimbiri chonchi kanthawi kochepa. pliz let this money go to hospital expenses for those that are needy.
Maurice had some facts misrepresented as expected from the journos. FAM has always been transparent and accountable but there are people out there deliberately twisting facts so that FAM is regarded as a bad egg. Its high time Malawians are told the truth that the National Team is a property of Malawi Government and as per charter signed in 1904 between FIFA and UN the Governments are supposed to provide financial support to the National Teams without interfering with the affairs of the Football Association who are like Governments’ agents. Once you understand this then it will be easy for… Read more »
Chonde boma lisapeleke ndalama kwa mbava zimenezi. Ndibwino mpila ulepheleke koma ndalama zipite ku ntchito za phindu. Mpira ndi bizinezi koma a FAM angoba m’malo motukula masewelo. Titha kukhala opanda national team. tiziwonela EPL, La Liga ndi zina zambiri.
ANTHU AKUMANGA MANYUMBA KUMPIRAKU ETI HOW COME 250 MILLION YATHA KALE VERY BAD
a ACB ntchito inatu iyi yochita kuwonekeratu.
Apatu pakufunika kafukufuku apa.
mavuto awa sazatha pa nyasaland
Ine zimenezi zimandiwawa muona pakatsala masiku awiri kuti game iseweredwe aboma apereka ndalama aaaaa!!
another cashgate scandal imeneyi koma zoliko zochita kukanila nchala hehedee uluuuuuu