Email a copy of 'Fan bruised with bullet gets hospital visit from Super League of Malawi official' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Fan bruised with bullet gets hospital visit from Super League of Malawi official' to a friend
TNM says it has paid over K58.5 million worth of Life insurance claims under its Moyo Cover insurance available to...
God have mercy upon him all the best and good recover .
Pepe neba! Sizon inonso wina akafa ku game yako!
Zonsezi zikuchitika chifukwa chosowa mastadium kumalawi kuno. Kamuzu stadiam ndiyasamunda ndiyakale.kuchuluka kwa anthu nkumene kukuchitisa kuti anthu aziphanachotele. ABOMA timangileni mastadium kwathu kuno mukutichitisa manyanzi.
Munthuyu samakawonera mpira anapitira zolinga zina, mpira unayamba nthawi yanji ndipo pamene amaomberedwa inali nthawi yanji. Kapena tinene kuti amadikira kulowa nthawi yamalova? Ndinali konko ndipo zandinyasa chifukwa ndinawonera kwa K381.01 change ku K500 chapita ku teargas chifukwa ndinangotuluka nanga mpaka ndidzikafa ndi teargas ngati inali game ya Bullets, ganyu yomweyi!!!!!!!!! Kkkkkkk
A chitsiru A Nthandalanda zikugwirizana chani ndi B4ward Wanderers fun komanso Walter ngati mulibe comment ya nzeru osangokhala bwanji
Izi zaku Malawi zitichedwesa bola mpira uyambike ku Europe basi tizionera wa azungu nanga daily anthu kukwapulidwa zoona izi
kafunseni ku Ndirande police za chigawenga chimenecho ndi zomwe anzake awachita a police omwe amachita patrol kwa Safa dzulo muganiza zongochibaya jakiseni wa ulendo
A nyasatimes, kodi mwana mumanena ndi uyu okula shaft ndi maballs eti. Hahahahaha
HE IS WAKUBA AMENEYU CHIFUKWA CHAKE WAOMBEREDWA. HE WANTED TO STEAL & TO DISTROY OUR GAME. GO TO HELL BB FAN.
SAD DEVELOPMENT