Email a copy of 'First Lady urges Comesa to invest in girl child education: To create an empowered generation of women' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'First Lady urges Comesa to invest in girl child education: To create an empowered generation of women' to a friend
The Effective States and Inclusive Development (ESID) Research Programme has commissioned a multi-country study on the comparative politics of public sector reforms (PSR)...
koma decoration ya nkhope ngati choumba mwa yenjeza mukufuna kuoneka ngati chani. ma ring mmanja dzasatanic!
Alwayz galz nt boyz! Koma lizakhalako bungwe loona abambo nd anyamata?
Kaudzudzu akanso inu!! Kodi ndi udzudzu wanji uwu wotchedwa Getrude Maseko Mutharika?
I am always surprised why African leaders take their wives to summits. Look now that it is becoming a trend to organize parallel so called First Lady summits which are practically useless. These useless parallel summits are an extra financial burden on host Governments
Girl childyo mwamudziwa muli ku Sanjika? Tamusiileni JB zimenezo inu simungazithe. Tangopitilizani zaulaiya ndi kukokola zinyalala mmadzalamu. Bola musabenso ku bungwe lina.Paja inu kukonda kuba ndi makani opanda nzeru. Mxiiiiew!!!!!!!
wat abt a boy child, unangokula ulibe nzeru
Awanso ndie amandinyansa bwanji,analowa m’gulu la anthu akuba,amunawo akutinamiza kuti ali ndi over K840 million koma kulephela kupanga ukwati kuchita kudalila anthu akufuna kwabwino,kulephela kupeleka ndalama ku mulakho,ndi BEAM mkuba ndalama ku NAC ndipo mapeto ake NAC ili m’madzi,kutinamiza kuti anakana salary increament koma pomwe amazidziwa mpakana Nankhumwa kulengeza,kutinamiza kuti Bingu adakali ndi moyo pomwe atamwalila,kuti namiza anthu kuti ndi Daniel Phiri, kutinamiza kuti vitara value yake ndi k51 m,ndi zambiri ndipo ndikuuzanibe,komano chomwe ndachiona nchakuti APM alibe chili chonse,mano alibe(mwina pano anagula) chisoni alibe,luso loyankhula alibe,mapulani otukula malawi alibe,ulemu alibe,nzelu alibenso.