Email a copy of 'Heavy rains, floods cause havoc in Mchinji: Maize gardens affected' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Heavy rains, floods cause havoc in Mchinji: Maize gardens affected' to a friend
Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development George Chaponda was subject to taunts and slurs in Parliament by Mzimba West MP,...
Chimanga cha mdimba ichi. Mvula yavumbayi ndi yobzalira chimanga kumene.
Nawo awa mukuti a Gumba awatu ndiye ai ndithu. Munthu opanda chitukuko kwa Mlonyeni ndi uyo. Mvulayi imagwa ali ku Lilongwe komwe amakhala. Izi ndizochita kumva osati zoona nthawi yomweyo.
Ohoooo my people!
@ Zoona zake! kukanakhala ku south bwezi Boma litatumiza kaye ma truck a relief items koma poti ndipakati …….ukuti bwanji?
Kukanakhala ku South bwenzi mukuti Mulungu wakwiya chifukwa chobera zisankho ndiye apa titi chani Tsano? Ooooh ndiye kuti chisankho MCP yawina posachedwapa chija inabera ndiye Mulungu wakwiya eti? Ndithandizeni amnzanga amene mumayankhula za mtunzu inu!