Email a copy of 'Japanese player jets in Malawi to join Wanderers: Genki Nakamura' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Japanese player jets in Malawi to join Wanderers: Genki Nakamura' to a friend
Premier mobile service provider TNM has presented prizes to pupils who have scored excelled in the Smart Kid game under...
Welcome Nakamula its nice to see u playing for the best club in malawi. Manoma 4ever.
Abutao ali wasewerako ku peru, brazil, germany, japan bwanji simumatchulanso za ku india, vietnam. Kodi mwati amasewera matimu anji? A social a premier. Ahhh inde ndakaika player uyu sangadutse pa fodya
Ubwere ndidzakutemere kaye before the training here in Africa we believe in a Sing’anga kupanda apo they will break your leg or you will be seating on the bench
Zoona takulandila and we encourage him to work hard
NDUDU ZIKUYALUTSANI IFE AMANOMA ZATHU NDI CHONCHI.WELCOME NAKAMULA.
Inu palibe zolalatilana apa,mvuto kumalawi aliyese amafuna kukhala pamtsongolo zomwe ndizosatheka, 1 amakhalapo modzi basi, enenu mudzibwera mbuyomu
Kodi neda osamayiwala kuti ndi Noma yokha imayamba zinthu koma osati zokaguliasa ndudu mu mseu ayi
Nakamura mpila wakuno umafuna ziwindi, udabwa. Sizaphada ukupangazo
Vuto lake wangonva zot ndi Malawi. Wati anthu ake samatha mpila. , nde mumulangize kt mpila wakuno umafuna ziwindi. Adabwa. Sizaphada zomwe akupangazo
Ife Wamanoma Tamulandila.Feel At Home Bro,most Welcome.Ansanjenu Tazigulitsani Fodyayo.Nyerere Woyeeee! Nkhawa Bii Anduduwa Mutha Chonchi-tu