Email a copy of 'Joyce Banda set to return to Malawi - Confirmed' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Joyce Banda set to return to Malawi - Confirmed' to a friend
Suspected shooter of former Ministry of Finance budget director Paul Mphwiyo, Macdonald Kumwembe, has asked High Court judge Michael Mtambo...
bwerako joice, kuno mkwanu, muluzitu ali ko kuno, ninga iwe, koma mwalimba mtimaa? bomatu is prepari ng for u kt akuninkhe nyumba, mukamva muti chan?Ameeeeennn,
Mbavayi ikangofika ipepese kumtundu wa AMALAWI poyenda pali ponse ndikutiuza ngati momwe ankachitira pogawa abakha aja.Mayi wamtunthu kumasiya office kumka namagawa abakha! nyansi yeniyeni!
Kwanu nkwanu mthengo mudalaka njoka.Muli wolandiridwa.
Bwampini wanu ndi uyu akulephera big time. Malawi is a failed state under a prof & Dr.
Zamanyazi eni eni winawe ukugona ndinjala koma ukunyoza amai…Uyambe kunyoza gogo wakoyo!! Viva JB!
kodi ku lumbadzi kulinso prison? its police cells. mind ur language fellas
Takurandirani omama boma likukoza malo oti mufikire mama kaya kumaula mwina ndi kulumbadzi kkkkkkkkkkk musova!
Welcome back mam! Government ikukoza malo oti mufikire kaya ndi kumaula mwina kulumbadzi musakha mam!
Now perfectly cornered. And her world has finally become small. And even the white man in America and in SA is ashamed to host a she-thief in joice. Bvumbulukani mai and Welcome to Lumbadzi Prison nanu mukalembemo kuti ‘Joice was here’.
The moment she don at chileka or Kia must be taken into the cell, no excuse and her fucken husband must be questioned for deformation. He failed to advise his bulshit prositute Joyce when she was busy insulting mutharika and the late now fwifwifwi talking nonsense,fuck you. She will stay together at chichiri prision amphaka a anthu
Muchita bwino kubwera kwanu mayi.