Email a copy of 'Judge Mtambo demands Kasambara’s comprehensive bill of health: ‘Conflicting medical reports’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Judge Mtambo demands Kasambara’s comprehensive bill of health: ‘Conflicting medical reports’' to a friend
A 37 -year-old soldier who was killed when when the vehicle they were travelling in, an Iveco Bus overturned following...
A Malawi koma, uchimo wamunthu wina ife kuwutengera ndikukhala oweluza? Ngati Ralph anachimwa ndizake, koma ngati anthu oopa Chauta mlengi, tipewe kufunirana zoyipa abale. Ada Kasamabara, ndikufubirani kuchira mwansanga, ndipo mukatero muzayankhe uchimo wa dziko. Madotolo muthandinzeni mubaleyu chonde, Dotolo Kalongolera osateketseka ndizinazi, ife okudziwani, sitikudera nkhawa pakuti inu udotolo wanu ndi mayitanidwe, amene simufuna kuluza patient. Ndukumbukila bwino lomwe 2007 mukundiimbira ine Junior wanu mumayitanidwe amenewa tsiku lililonse kupanga check ma patient anu pamene inu munali kunja kwadziko pantchito zina. Quick recovery Ralph
Don’t worry about rk as a lawyer he knows what keeps suspects out prisons cause the law will accept it he knows what could prevent him from imprisonment so he will make all the tricks to avoid going to prison but rk knows the source of his bravery if its not a good source he will be punished heavily by the true lawyer coz everything is being recorded in heaven it is possible to say father God forgive me and save me by reciting all his wrongs on the other hand if it’s a good source of braverly thank God… Read more »
Lughano you are a surgeon, am i right? Is Ralph’s condition surgical?
Anyongedwe mbava chitsilu chimene Chija bolanso chingofa
Ralph aise! Be a man and face your demons! Look at your friend Lutepo, he tried the same trick koma anamukwidzungabe!
Vomera machimo ako!
Lughano mwana wakwithu, wa seventh day, msilikali withu.Chinyengo sichabwino mwana iwe leka. Musiye Ralph afere zake uyo. Iwe ukulemba report ngati ndani? In what capacity? Lughano! Lughano! ndi u specialist wako wa fake wo, wopangira pa CoM. Ka college ka fake kamene tsogolo lake silikudziwika
Crime is a crime. The Law of the land should treat us equally. For decades, there has been a partial system of Justice in Malawi where by only ordinary people have been facing the law, whilst the optimates have been flying above like Eagles, yet they are the ones who have been committing serious crimes.
People, I sympathise with the Kasambara family at this tough moment. Kasambara is in dire pain. If one is able to malinger to an extent of having fever, low blood pressure and needing oxygen, then Kasamabara must be a genius deserving an automatic entry into the guiness book of records. Let him recover and then justice can take its course, lest the whole setting by Judge Mtambo is viewed as a personal vendetta at Kasambara.
kkkkkkk…why makhumucha akangomangidwa anvekele;ndikusegula m’mimba,mutu waching’alang’ala,iyayi ndatota nyere zikundipweteka and ………kkkkkkk…why?…ife amangotikoka ngat mbuzi or kutipeza tikudya amatisiyitsa phwanya,ok oweluzadi ndi chauta osat ma………..
Kodi chifukwa chani andale amadwala ikakhala nkhani ya milandu? Remember Yusuf Mwawa? Bakili Muluzu? Ralph Kasbara? Very sick mpakana kufuna kufa, koma milandu ikatha matendanso amalira penepapa. Joyce naye akabwera straight ku Mwaiwathu bp