Email a copy of '‘Love story’ turns fatal: Man commits suicide by hanging from tree' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

87 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
uthixo ukhona
8 years ago

zaziiii zochotsera moyo, akazi kutapa kutaya oti sunakumamepo nawo. kungokumana kumachita kufunsa kuti kodi unali kuti nthawi yonsei

Chisomo
Chisomo
8 years ago

Straight to hell. Hell is real. Gehana ilipodi.

INNOCENT
8 years ago

KUMAONA GUYZ ZISANAFIKE POPWETEKA CHONCHI.

ETHELMACHESO
ETHELMACHESO
8 years ago

Ndichitsiru

Binton wakale
8 years ago

Mkaziyu ndithu kalipo kamene mubaleyu anagomera moti amene akwatireyo basopuu.Anyamatanu osafoyira zilizonse ngati kudziko kuno kulibenso wopambana.Ndipo kawirikawiri ilili ndivuto la amene safuna testing first be4 marriage inde ndibwino koma umafoyira ndizozizira.Moti uyuyu akanakhala chiwomba nkhanga unali mwayi wopeza buthu la tsopano ndipo timasankha chimupweteke aphunzirepo kanthu.Namwali uyu basi matama mbwee kuti ena anaferapo pa iye.Makolo nanu muzimvetsa mwana akakanika chivomerezeni mwapha waweni apapa manyazi akugwireni ndipo aliposo ena phunziro ndilimeneli chonde chonde.Mwana wabwinoyu basi wapita ndiye muona amene agwire wanuyu kunyatsa nkhope azakusekani okuzungulirani kuderaro.kaya

nya
nya
8 years ago

Kape iwe m’mene umati ndisova man, umanena kuchotsa moyo choncho. Mpaka 6 ft down nkhani yake yomweyi. Ngini zonsezi. Wosapeza ngini ina bwanji. Akuluakulu ana kaya amuna kapena akazi ngati ali ndi mwayi wakugonana kuli bwino kuwasiya maka anyamata. Chifukwa amaphunzira at least 80 percent of tricks for love before marriage. This is very good. Ada awaadalowa m’banja asagwire ngini ina iliyonse. Thus why suicide was a right solution as he did not want starve hi dick from sex.Man you could have come back to masturbation. After all masturbation is better than ngini.Ine ndinapeza wanga koma nditakhumudwitsidwa ndi ngini zosachepera… Read more »

Zangazatha
8 years ago

Kuganiza kwa Chichawa uku

Faith
8 years ago

MAKOLO OSAMAKHALA NDI MTIMA WODALIRA. KULEMERA NDI CHIKONDI NDI ZOSIYANA. MWAZI WA ADAWA MAKOLO MUKAYANKHA.

abit nyonyonyo
abit nyonyonyo
8 years ago

in ths earth, nobody was born with money. it seem these 2 luvd each other. mind u akuchikazi chikondi si ndalama. adzakwatila ndi olemela mwana wanuyo koma ali opanda chikondi. mudzafa imfa yowawa kuposa iyi

velo
velo
8 years ago

If you faint in th day of adversity, your strength is small…Proverbs 24:10…let God increase our strength in times like this, to avoid more loss…

Read previous post:
Satanist claimant arrested in Mzuzu: Malawi Police says he is trickster

A 25-year-old man, Stanley Nkhoma is currently in police custody after he failed to con a Church of Central African...

Close