Email a copy of 'Malawi angers UN over misuse of HIV money, risk losing Global Fund help' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi angers UN over misuse of HIV money, risk losing Global Fund help' to a friend
“If you judge people, you have not time to love them.”-Mother Teresa At any cost an army is supposed to...
Koma Pitala mpakana zina kupatsako Gyan
a Malawi kusamva komanso kusachedwa kuiwala…dont be cheated kuti ndi amayiwa ndi Mamunayi .musaiwale Mkuluwake amachita chimodzimodzi kumatenga ku escom,malawi savings bank and many more tonse tinawona komanso kumva .mkaziyi wabwera liti kuti akapeze mphamvu zoterezi ….to me i rule it out the its Mrs, its Mr himself……kugwiritsa ntchito udindo molakwika…..kukagwiritsanso ntchito molakwika.
UNAIDS should not try to be holier than thou. They have also been milking NAC through their bogus Protect the Goal Campaign Project. They took money for Asamoah Gyan and also for a number of Ministry of Youth Programmes. Copies of the payment vouchers are there. NAC should respond to this if it is not true. The UNAIDS Commission Summit hosted by Joyce Banda also took over K50 million. Akhale chete amenewa!
The money must be paid back.
BEAM = Cashget
Za AIDS zokhazi bwezani. You have crossed the line. Apo bii! timatcha.
zoona inu a nac mukapeleke 5milion ku beam,mwaona global fund will hold its funding,dpp ndiyakuphadi pano mufuna muphenso anthu oti akuzigwirira ntchito ali ndi hiv mukupeleka cash ku nisb kuti chani ku mulakho why giving that stupit grouping anthu ozikonda,ndalamazo mubweze ngati mukutumikila anthu refund,koma ngati mutumikila zinyama zidyeni anthu tife amene tili pa treatment,agalu angulu inu simunati pitala ali ndi ndalama bola amai or mukanamusiya Chakwera alamulire bz is the one tikudziwa kuti anawina,zonsezi ndi mkwiyo wa Yehova zinthu zikudula daily
Kukhala mai sichifukwa.Boma la Joyce Banda linayesetsa kufukula cashgate ndikuyamba kuzenga milandu mbala zonse. Peter apa ndiye mwaonjedza mpaka kuba ndalama za Global Fund? Musova
Zochitika Ku malawi zingakupange munthu kusiya chichrisitu ndikuyamba kutukwana. Nanga zoona mabungwe atatuwa achita pamenepa si cashgate imeneyi. Kodi a Dausi ndiye kuti mukudwala edzi limodzi ndi Mayi Bwampini? Bwanji mukufuna kusokoneza ntchito za edzi mdziko.
Kangaroo ndikanyama sangakhale munthu.
NAC gate