Email a copy of 'Malawi govt to stabilise maize prices: Mutharika seeks international help' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi govt to stabilise maize prices: Mutharika seeks international help' to a friend
Southern Region Football Association, the runners of Malawi’s second tier league have described the sponsorship from Nsejjere Sports Wear and...
Mulungu akufuna tiphunzirekuti andale ngolephera,lawo ndi bozabasi.Anthu m’mizimu alibe kalikonse olo mwanapiy e nde chimanga adzakwanisa kugula?nanga fizi azaitenga kuti? kodi wosauka kumalawi alibe sogolo ?nanga tsogolo lawo ndilotani?Inu andale ndi atidwenawo okonda kululutira ndipamaliropomwe samalani kumwamba kuli Mulungu.Osaiwala kuti amlanga ozunza amphawi ndi amasiye,mukumbukire padzana,amwano amawatenga mwachangu.
Malawians this is a sign of doom, why is the DPP and Muntharika’s take as for a ride Bingu didi the same here is pitala, tionkanena adathira msiidzi ndi izi lero…think twice
Iwe no. 2 ungokhala chete umadziwa momwe anthu akuvutikila ku muzi kuno. Iwe ukudya kumeneko uli phee nde ukunena za nkuto za ziii. Osangovomeleza kuti zinthu zavuta bwanji?
abale koma tipulumuka?kodi iwe voti yanga sinapindule
It is of great significant to stabilise maize prices for the vulnarable
25,000.00 /50kg
koma tilimba??
No one will die with hunger inu muvekele heee munya muvesa njala ilibe masewela.We have plenty of maize inu matako pasi today the same person is telling you to ask donors to help for maize A Malawi ambiri mitu yanu njoduka mulilira ku usi
Let’s solve this amalawi…ma kakileta mmanja tonse.. List of feez in various school here in malawi arccording to malawi government 1)-primary school=k950 per month 2)-seconday list nation secondary=k85000 district secondary=k35000 CDSS=k11000 3)-colleges list TTC=K35000 Domasi college=k220000 unima=k270000 other university mzuni=k275000 Bunda=k280000 NRC=K190000 NO GOVERMENT INVOVEMENT IN FEEZ PAYING BECAUSE GOVERNMENT HAS NO MONEY TO Assist paying fees NOW THE GOVERNMENT IS TALKING ABOUT STABILIZING MAIZE PRICES. the point is chikukwera kwambiri….ok fine nde masamu nawa If my reading servers me right 80% of Malawians leave in rural areas and are peasant farmers. which one can also concluded that a big… Read more »
Guys mwati K2milliom or ‘k200million ,or ‘k2billion ,I don’t think the whole President can say that it was just a mistake ,K2,000,000 /7 =285714 bags
That’s the way to go Prof. A.P.M our first citizen. Do the needful for the long term benefits of Malawians. As much as we appreciate your efforts by firstly purchasing the maize that is in most Admarc deports please let’s teach Malawians how to fish on their own. Tisamakule ndi mtima wodalira. During the elections you promised good policies to alleviate hunger in Malawi. Where are with the implementation of such policies? Let’s donors and other partners best ways to sustain our stomach on our own. Anthu ayiwala irrigation. Let’s do irrigation mwakathithi. Apaseni ma materials ofunikira in good time… Read more »
Iwe antholok ndiwe kape galu pali choyamikila apa pamene anthu akuzunzika. Swayin pusi opanda nzeru. Kapena iwe ndiolemela sukuona vuto? Shut up your big mouth.