The gate system is in our blood,ngati sukuba kuntchito kwakoko ukufoira cz aliyese panopa ali ndi gateblood even onse ogwira ntchito ku mbc mbava zokhazokha,and writer of this article was dished out for the whole story,,,,,,praat kak!!!!!!
yakunowa
9 years ago
A Mbwenu ndinu opusa. Nkhani ili apa ndi ya serious and inuyo mukukambapo zanu za mitundu. Kodi munakhala bwanji anthu openga inu?
On the issue in the story, I am also surprised that the number of music downloads for certain musicians is going down. From my limited knowledge of IT this cant happen unless there has been an overnight technological advancement which some of us are unaware of. The worst that can happen to one’s number of downloads is for them to be static.
zomwezi
9 years ago
And why putting ur music on a non paying website, u should get something for your luso bwana.
Waste of talent and time with Malawi-Music.com
mbwenu
9 years ago
nkhani ili apa ndiya gwamba chifukwa ndi mtumbuka nzanu a nyasa simumatha kulembaso nkhani inu naga mwawafunsa a malawi music downloads kuti afotokoze kuti chikuchitika ndi chani?….mbuzi!!!!
lady gaga
9 years ago
Za ziii, khalani nazo nyimbo zanuzo, tikatsitsa anaconda wa minaj pa youtube. Komanso Johnny
keputa
9 years ago
hahah…the author of this article must be a stupid fool infact a useless dude…. what happens in music downloads is that the rate of a song & number of downloads are determined by plenty of factors one of it being the release date… consider Gwamba’s bola kusache single..how many downloads does t have up to date? f t z not close to 40 000…but z t on the Malawi music’s top 20? the answer is no bcoz t wz released way back… xoh n most websites after a week passes all the downloads of that song n that week are… Read more »
Keputa you sound like one of them and to me, a big joke is you brother it seems you dont understand whats being said. Tikuwuze muchichewa.
Zomwe wakamba kuti zimatengera ma week ndizowona koma how do you explain the deduction in downloads.
I have checked ma snap shot aise and nyimbo ya Gwamba ukunenayo ma downloads akutsika. inali pa 13 thousand now ilipa 9 thousand. IT yanu imayambira ma downloads ambiri nkumatsika?
Dont blame nyasatimes ayise akungotiuza zomwe zimachitika zomwe ambiri samadziwa. This is investigative journalism that most journalists couldnt think of and being supported by proovable facts.
zedediya
9 years ago
Inetu ndimadabwa kuti kodi nyimbo izi ndiye zititinso akuti Malawi’s top 20 chart! Ma downloads a fake. Umbava pa Malawi uli paliponse nowadays. In the name of promoting Malawian music. he he he
Moto Wayaka
9 years ago
Safety sili safe, mpaka fote sauzande zomwezi?
Dumisani Chikadya
9 years ago
This is very true, I just downloaded a song and I expected the figures to change automatically (as they should) but nothing happened.

Mazoba awa tinawona kale ife khalidwe limeneli ayini ake amati.akupusitsa amalawi.