Email a copy of 'MCP calls Malawi economy ‘ouroboros’: Tears ‘leprosy’ budget' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP calls Malawi economy ‘ouroboros’: Tears ‘leprosy’ budget' to a friend
Blantyre based IT specialist Wisely Phiri has been elected president if ICT Association of Malawi (ICTAM) following elections conducted during...
Akaletsa kuchita import ma toothpick ndi inu nomwe muyambe kunena kuthg taonani ndi ma toothpick omwe sakupezeka.muyambe kupanga ma toothpick of comparable or higher quality then things will sort themselves out no one will import them.
So what’s the alternative to the monetary policy you idiot!
Anthu mulibe manyazi eti? nungalangize kuthukumve ngati Bwampiniyu? kkkkkkkk
where does namaan&reprosy fit in economics azimwale?
Kikkkkkkkkk!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! azungumbuli mwati bwanji? ku chemerela umachemelera yako zimenezo inu muzidziwa!!!! ifetu timanyadilana munthu wathu akachita bwino kutoteroko mkunyadila osati poti inuyo mwanva kuwawa ifeso tinve kuwawa yayi kwathu kuno kulibe zimenezo mwanva odala?
Ndakunverani chisoni chifukwa zikuoneka kuti nanga ka mtima kasanje kakulapo, ngati palibe nsanjeyo ingokozekani nsanjeyo yayandikila ndipo ikugwiritsani ntchito ndi nkwiyo……………………………………………………………!
Ngati mwakwiya kwiyani zeeeeeeeeeeedi tsono!!!!!!!!!!!!! kikkkkkkkkkkkkkk!
a Dzonzi tawaudze zoona anthuwa nkhutukumbwe
Mbvekere” ndilibe problem” Zoona!
Heheheh
This MCP guy has a problem! He is a Malawian. Let him propose something that he thinks is feasible for the country. This is our nation. Whether DPP, MCP, PP we are all Malawians. If you think we can vote you in power because you are a good oppose but you never suggest what is feasible, FORGET. Muzingosutsa choncho.
Inu amene mukuti mwana wa Mchewa ameneyu ndinu munthu WOTSALIRA ndiponso WOMVETSA CHISONI. Tribal affiliations have no place in civilized world! Mupindulanji ndi mangawa osankhana mitundu? One is not brighter because he is a chewa, Lomwe, etc! Wake up!!!!!
Zoona m’meezo nde kuyankhula kumeeko odala. opulezident wathuwa sowerenga buku lopatulika kuti okadziwe zinthu ngati izi. Mouze zanzene kuti onvetse. Inu ndinu patali onyata o ku Dowa.
Thats very true, there are alot of Bible stories to learn from, and indeed our Leaders need to humble themselves like Namaan the leper. Teach Peter Muthalika alot more Bible stories coz he doesnt read the Bible.