Email a copy of 'Mr President, nili na pulobulemu: Malawi situation' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mr President, nili na pulobulemu: Malawi situation' to a friend
Malawi and other developing nations will be sidelined from World Bank funding in projects that could end up harming gay...
mcp?? musamazivute simungazalamulire dzikoli……… a DPP ma pulobulemu tilibe so what??? iyaaaaa munya apumbwa DPP mpaka twenty sate chani uko wooooooh
APM got the timing for his ‘joke’ all wrong.
Those who knows everything was not asked all questions.
I used to respect Saulosi Chilima but now I have noted that he is just another lizard on the rock. I remember in our village we had a cowboy by the name Saulosi. I think Saulosi you are a cowboy other than a VP.
Uyu ndi wachamba guys
Chilima lost me the day he called ma an idiot. I am sure he has lost many other others.
In fact he has called my poor, starving mother an idiot for complaining about the hunger and other problems in Malawi affecting her. I cannot have any respect at all for anyone calling my mother an idiot.
tinkanena ife sankhani mcp, anthu awa alibe napuloblemu,ife amalawi ndiye tili ndi maproblem, uyu mavuto athu siake.
l love Mr President. love him he will do his best.Malawian we have problems we nid answer the same time we ask learn to be patients
Ndinu ochita bwino eti, what kind of patience do u want, let me tel u this mavuto sazoloweleka
palibe amafuna mavuto,sakuyankhula bwino ngati atsogoleri.
Saulos Chilima, iyi si Airtel, ndi Boma. Ngati nzika za Malawi, tili ndi ufulu woyankhulapo pa zonse zochitika mMalawi. Zowona iwe unaphunzira za Economy. Koma udziwe kuti kuphunzira za economy sikudziwa economy. Siapa Pitala ndi iwe mwalephera kuyendetsa Boma! Boma mwaphwisa nalotu, mwanya nalo!