Email a copy of 'Parliament approves Kachama as Malawi Police chief' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Parliament approves Kachama as Malawi Police chief' to a friend
Malawi’s former Ministry of Finance budget director Paul Mphwiyo told the court that that former Justice Minister and Attorney Ralph...
Congratulations a bwana Kachama. Mulungu akuyanganireni. Mwayamba bwino poyamba kumanga anthu a ma bottle store amene akupitiliza mpaka nthawi yochedwa ndi kuimba music yosowesa mtendere anthu. Ma bottle store a kwa Mananse , Nancholi ndi Manytowe. Zikomo bwana. Anthu a madera amenewa apeza mpumulo. Pitilizani kuwamanga. Ndikhulupirira mufikanso pa Kamba pamene pamakhala chisokonezo zedi. Ma galimoto amapangidwa park mu nseu blocking other road users. Ngakhale chigololo amachitira pa nseu pomwepo- chopolama pomugwiritsa mkaziyo tayala ya galimoto. Njansi zeni -zeni. Please stop this madness. Ku Kanjedza pa ma bottle a Chisesele kumakhala disco ndi phokoso 24 hours. Police cars are packed… Read more »
Congratulation bwana Kachama so you better praise God and we shall pray for you
UNIMA inali kale people prefer to send their children abroad or atasankhidwa ku UNIMAyo.
Which means Shareworld is total disaster
Zabwino zonse abwana. Koma musayiwale anyamata anu mbuyomu.
A Bwana gwilani ntchito momwe mumagwilira muja. Inu musakhale spokesman wa police ngati ena aja.
Zoona akumudziiii…….Congrats…
Bwana IG, ndinamvera nyumba ya malamulo momwe inakukonderani, ndichifukwa chamakhalidwe abwinno. CONGRATS. mupitirize makhalidwe abwinoo.
Congratulations are in order bwana Kachama. Ine Mphunzitsi wanu wa Research Methodology ku ShareWorld Open University. We will talk on phone.
Zabwino.zonse
IG koma uyu