Email a copy of 'Police impersonator arrested: Swindled Malawi entrepreneurs' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Police impersonator arrested: Swindled Malawi entrepreneurs' to a friend
Hip-hop sensation and producer Dj Kali has released his new single “Love U Better”. The song premiered Monday by Malawi’s...
koma ameneyi….kkkk
I know the guy akulu ake ndi a hospital director ku trinity hospital
How can SMEs improve if police which was supposed to provide maximum security impersonate entreprenuers? Shame police
Ameneyo musamusiye choncho eeee azolowela
Akagwire jele ameneyo anayambila kale wadya zambili za anthu
Balaka and Mchinji………. maboma amenewa bwanji???????????????????????????
Anthu awa amalimba mtima coz amakhala atayamba kale zinyengo kudzera mwa apolisi ena osakhulupirika.Lero uziona ukuimva bwanji selo mphwanga? wapolisi wodzipatsa wekha in new Malawi no chance.Tamufufuzani bwino mwina alipo ambiri mpakanso IG wao alipo,mumkhaulitse.
Kuwufunitsitsa u polisi kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Akuba amenewo musawasekerere….amangeni basi.
Bwanji osapeza zina zochita? Ndi murandu ndithu