Email a copy of 'Political scientist faults Mutharika for declaring to run again' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Political scientist faults Mutharika for declaring to run again' to a friend
Atlas Energy Limited, a Malawian company with interest in solar power generation, has given Blantyre Press Club (BPC) K1 million...
Mpuno ngati belu la kachisi
Yes skip the email and name
Musamvutike naye ameneyo tione mmene afikire komwe akutchulako
Zavotere anyamata akowo ife timavotera mvundo ndi madolo opititsa dziko lathu patsogolo, mikhula ng’ona yachitukuko, yosapangira nsanje makampani achimalawi
NGATI MUKULEPHERA KULANKHULA BWINO PANOPA MULI NDI ZAKA 75 BWANJI MUKAFIKA ZAKA 85? WE ARE TIRED KULAMULIDWA NDI MAGOGO!!!!!!
Afiti, athakati, anthu amphamvu za kumidima inu a opposition mzeru zakutherani tsopano mwayamba yanu ija yotemberera munamukomola nayo Bingu ija, mpakana mavesi a m’Baibulo zomwezi, zandale zomwezi mpaka kumamudulira mzanu malire ayi Mulungu akudalitseni ndipo umbanda wanu ulendo uno ukutsamwireni nokha. Kodi iwe Hussein ndiwedi kadaulo weniweni koma? Why not giving us the true reasons why APM is on the wrong side of the law by showing interest that he will stand again in 2019? Before giving your opinion as the UNIMA political expert, did you come up with your thorough conclusions to why APM said such remarks? What has… Read more »
Akagwere uko kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk !
TRIVIA TRIVIA TRIVIA!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Usawi chichi?
Barabas unleashed!