Email a copy of 'President Mutharika joins thousands at Bingu memorial service' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

21 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Kasia
Kasia
7 years ago

Anthu akumwalira kaamba mankhwala mulibe mzipatala,koma boma likuonongela ndrama chitanda chakale kale?ufiti umeneu!!

Tione
Tione
7 years ago

Anthu akufuna mlatho ku Rumphi uku & you waste so much money for remembering a dead thief! May God punish you for such useless memorials! Anafera zake uyu ndi Penumulungu! Mudzasowa chowilingula ndith!

Dum Magulajena.
Dum Magulajena.
7 years ago

Peter mantha sangalankhule pa mwambo wa maliro ndi mnyamata kaya iye uja si wangokwatila pompano Getrudeyu ndiye chibwanabwana chidakali chonse!!

zuzo dekha
zuzo dekha
7 years ago

THESE ARE TWO BUGGERS. anangoitanana kuti m’bale cokako ku US bwera kuno kuli mbuli tizazimete.usacedwe. pitalayu anali busy dzana lija za visa yake , ai ana anga awa, kaya anakawatenga pati pena a mu ZIM mu ana azakhali ake, samaoneka pa US standard mmene amaonekela kazisamalidwe kake. basi ife kukhulupilila. THESE ARE TOTAL DAYLUGHT THUGS.tikamazazindikila atapita.
za Calisita posapatsidwa mwai olankhula, mwina angopangisa misa ku ndilande.kkkkk.
ma gold digger awa step mother wa CHACHA . heeedeeee

zuzo dekha
zuzo dekha
7 years ago

kunonomala
why spending so much waste of money for the occassion? nde wauka???????????? why are we doing this. tose timaziwa olo tikapanga cikumbuso mmamizimu, there is lots of money we spend ,then come to this so called boss of ndata how much do we spend< fuel,maluwa ,zovala , ma allowance ku malilo ,zokumwa ,olandila alendo, oseca, lolololo ma allowance, ndithu kumwa mikodzo ya bwana otizuza. bwanji zimenezi azingodzipangila a kubanja than spending all this shit of money? ose a mmidzi anabwera ,pobwerera kukafikila pa njala. total brutal and nonsense.
mapemphero basi is enough not all this SHOWBIZ

massa wasowa Andrew.
massa wasowa Andrew.
7 years ago

if u dont know anything just keep quite coz we ‘re not all stupid who read this nws…

mbwiyache
mbwiyache
7 years ago

Kodi chief mourner, namalila wamkulu ndi ndani pamenepa? I have never understood why in all these memorials, the surviving spouse Madam Callista is marginalised. Mumamukumbukila pa nkhata poti pamenepo mu ma jama. You have DPP officials kuyankhula, and yet olo kufunsa oimila kwa Madam Callista or even the former first lady amene to speak and celebrate her husband’s life. Shame. Chikumbumtima mulibe.

winston msowoya
winston msowoya
7 years ago

Prolific words DZAMBO.Why should the impoverished people waste their time and energy remembering a thug who stole billions of KWACHA from government coffers for his own interests,while the people are facing atrocious poverty,lack of drugs in the hospitals,shortage of power and water have become a norm the list is long.No Malawian with active brains,would cry for this demon who is now languishing in the sea of inferno.These two rogues came to Malawi to exploit and enrich themselves and members of their families.By the way,where did these thieves come from? We could have learnt a vivid lesson from Banda.As it is… Read more »

Haward mulolo
Haward mulolo
7 years ago

Get out mtumbuka

CHIM
CHIM
7 years ago

Anapeza banja
Basi

ALIBE POLOBOLEBU !!

Kafuse
7 years ago

Muzafera Kususa Kwanu Komweko Boma Simuzalinukha Agalu Inu

Read previous post:
Parliament rejects controversial Chief Lundu on MBC Board -Report

Public Appointments Committee (PAC) has rejected controversial Paramount Chief Lundu to be part of Malawi Broadcasting Corporation (MBC) Board after...

Close