Email a copy of 'Student hacked for stealing sugarcane in Kasungu' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Student hacked for stealing sugarcane in Kasungu' to a friend
Police side Blue Eagles demonstrated why they could be one of the favorite teams to lift the TNM Super League...
Nthawi zina ana sukulu do not have discipline for these villagers toiling in their farms close to their schools.Sometimes they are so abusive in their languages when they take cheap liquor of kachasu and start stealing these people things however the punishment meted for these wayward boy was too heavy for him.Students are supposed to be at the campus studying and eating whatever the school provides them than stealing from the villages close their school.Extra food is the responsibility of their parents sending them extra money.
Iyaaa mwana asadyeko mzimbe mwini munda walakwitsa.
@ 1(Msalanyama vge,)njala yavuta kumeneko, koma mwini munda amasulidwe as soon as posible.children MUST BE GUIDED kuba sikoyenera .Alangidwe basi mwanayo.kuti ena aphunzirepo asaaaa.
Comment kukhala ndikanapheratu inu kulima nditchito maka kutsegula dimba wakhaula a polisi sadziwa kulanga koma amngonyengelera.
Mwini DIMBA walakwaso chani? zinazi mmmmmmmm!!!!!!!!!!
..Zadziwika kuti apolice mukulimbikitsa umbamva, chifukwa mukumapereka malamulo onama, kusiya kuona chomwe chatsitsa nzaye kuti njobvu ithyoke mnyanga…..
Umbava ouyamba ali mwana! Too bad, God heal our land
This is the problem with most of scholars.The time there fellows were busy stuying,these stupid boys couldn’t hold their wickedness.If I were the owner of the farm,I could have amputated the leg as apermanent lesson.
kkkkk…mwina sukuluyo imaphunzitsa kuba
Boma la Malawi ‘muguliletu chimanga kwa Maiko anzanu chaka chino cha 2015 kukhala njala yoopsa… akubawa asulukanso… njala 2015….