Azimai chonde phunzitsani ana anu makamaka awa akaziwa kulira maliro. azimai kukhala ngati amuna olo dotho la misozi……….. RIP vic
llonzoh
8 years ago
may his soul rest in peace
chatonda
8 years ago
I really wonder with the behaviour of Seodi White, what is wrong with this woman? She is fond of doing bad things in public. She is dressing very awkward and rudely yet she is attending the funeral. Pepani mai you willl never find a husband to suit your bad behaviour.
Tasinthani khalidwe please. You are popular for bad things all the time. Reduce speed please and let to respect events depending on their nature. Go back to the saloon and have your hair redone.
Alfred Minjo
8 years ago
Minibus Driver???? pongofuna ku muyalutsa Victor White Mbewe, MP wa DPP. Panali nkhani yopereka profile ya MP pamenepa pa maliro amunthu wankulu ngati ameneyu Victor Mbewe? It was enough saying Victor Mbewe MP is not Victor Mbewe a successful Banker. A chair, mpandodi wakumaliro umenewu? Muli neng’aaaaaaa, kuumvera bhoooo…. Nanunso a Seodi ndi amai enawo apaka milomo ndi zofiirawo, mmmmmmmm! magalasi akumalirotu amenewo? Koma abale miyambo yamaliro tsopano ikulowa pansi zedi……Makolo muli kuti mutichotsere ntonzo ngati uwu chondeeeee!!!!!
BONGIE
8 years ago
Its time.
citizen okwiya
8 years ago
@ Prisoner Monger
Good observation for man onyamula portrait, he is the one bro
Brian Kapindi
8 years ago
Indeed Life Is Short! Rest In Peace Vic!!
anadimba
8 years ago
may his soul rest in peace
Prisoner monger
8 years ago
Observations :
What is the significance of kuvala za black pa maliro?
Izi zomakhala ndi manda muma residential areas zimasikoneza afiti
Zimagalasi zomwe wavala Seodi ndi mzimayi wina yo not suitable for pamaliro
Kodi mdala uyo wanyamula nawo bokosiyo, si uja amene amkanyamula chi potrait cha Bakili Muluzi ameneyo
Rest in peace Mr Mbewe my boss Father