Email a copy of 'Wanderers 2-2 with Blue Eagles: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers 2-2 with Blue Eagles: Malawi TNM Super League' to a friend
The Human Rights Consultative Committee (HRCC) has asked Malawi Congress Party (MCP) to denounce insults and racist attacks its law...
Masapota a Wonderers ndiwo ma savage coz anaphesa munthu Ku balaka chifukwa cha ndeu, anayendesa ma players awo pansi Ku MZUZU, kuchosana pa udindo osasata constitution ya team. Usavage udutse APA.Zakukanikani matama thooooo.Mwayiwona Bangwe
Zizayenda tym ikadzakwana
Neba wakhala ukuluza mbuyomu kufika pomanena kuti bola kusiya kusewera super league chifukwa mumasewera ma games ambiri. Ife sitimakunyozani chonchi. Anthu sanama akamanena kuti timuyi yachuluka masavage. Tisiyeni ife Manoma ndi Manoma. Tikudziwa kuti tsiku lina zidzatiyendera.
I love manoma for eva
Tili nayo nga,nga,nga noma ife
kodi mufuna adzachite kukuvoterani mu std cup
ehe chitimu chomvesa chisoni
I Love Nama Mngakhale Sikuchita Bwino
Manoma oyeeee zivute zitani tili pa mbuyopo chi team cha anthu ozindikira ichooooo
Neba khala chete iwe cup watenga kale. Nyerere ndi Nyerere basi.