Email a copy of 'Admarc board sends Mulumbe on forced leave over ‘maizegate’: Mauwa acting CEO' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Admarc board sends Mulumbe on forced leave over ‘maizegate’: Mauwa acting CEO' to a friend
Director of Public Prosecutions (DPP) Mary Kachale has said the prosecution will prove its case on how Cashgate was schemed...
DPP = DEAL PAFUPI PAFUPI
HEEEEEEEEEEEEEEEEEEE ALOMWE ALOMWE
I see that the ADMARC Board is showing much better leadership that our president. Kodi munatontenga kwayani ameneyi? Koma atotikwana bwanji. Asaaaaaa.
Mr president could you please suspend Chaponda otherwise apa a Malawi tiziti izi nzogwilizana nonse ndinu mbava.We are tired of DPP Govt.full of thieves.
Tsopano Ndiye Nayenso Chaponda apitetu ku forced Leave Nanga kungomuthothola Mulumbe basi. Mafiozo nayenso athotholedwe.
Time alone will tell. Dzikoli ndi anthu ake mzaYehova wamakamu.
Galu wakuba weniweni ndi Chaponda. Nayenso achoke to pave way for investigations. Ngati amaganiza zoti adzalamula Malawi achotsele. Akalamulila kwawo konko. President samakhala wonyansa chonchija. Kunyansa nkhope, maganizo, chilichonse
Let this big fish also go on leave, why are you shielding him? Am asking Mr.
President.
Chaponda and mutharika are in the same boat…of stealing from government coffers. ….
No no no no mtsamilo uwu! Chaponda achoke!
Zinazo mbuyo!
APM & Chapponda ayudas enieni a dziko la Malawi. Anaba mavoti pano akupitiliranazo. God sees u.
KOMA PAMENEPO ACHIMWENE MWANENE ZOONA ZEDI