Email a copy of 'Airtel Malawi in job cuts: 41 axed in ‘repositioning move’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Airtel Malawi in job cuts: 41 axed in ‘repositioning move’' to a friend
Afro rapper Piksy real name Evans Zangazanga has said he is ready to dish out the best ‘Valentines show’ in...
Mwangotichitila atsikana athu , lero mwati muwachotse nchito. God will punish you.
Koma violet chonde musamuchose, wachindisa kwambiri kwa mabigi. Nyina yatupa modesa nkhawa
Cry my beloved country…
Please tread carefully this time around. There is a pending issue in Supreme Court of Appeal which you already lost at the lower court. The issue involves those you retrenched a few years ago with a meagre package. How can you retrench someone and give hime or her K600,000 as a reward? Airtel is full of headless chickens. I hope Bridget Jumbe is no longer there. She was the masterminder of the previous retrenchment.
Kuchotsedwa ntchito sizachilendo,ndimmene zimakhalira
Anthu osogola sagwira ntchito ndi makampani achimwenye.
Ntchito amachotsana January? Komanso mmene ikuyendela economy anthu apita kuti? Kulakwa inu. Mmene munkawalemba simumadziwa za repositioning zanuzo? Mwagonagona nawo atsikanawa! Nanunso atsikananu kutengeka….inu simumadabwa kuti anthu a maphunziro ochepa koma ntchito mukulembedwa
This is terrible news i tell u, what is happening in Malawi? people losing jobs that way?
Paja kampani yi ndi ya ku India? Ndiye ntchito za mwa amwenye, zimatha chonchi.