Email a copy of 'APM pays Kamuzu posthumous tribute: Malawi marks 17 yrs since death of founding president' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'APM pays Kamuzu posthumous tribute: Malawi marks 17 yrs since death of founding president' to a friend
Mulanje Mission Hospital staff, who claim to have suffered and trampled upon in silence for a long period, have penned...
Koma mpaka pano you are failing to honour his pension. Angulu osayamika, mkulu wanu uja anapita ku college ku india on ngwazi’s sponsership but u can’t stop calling dictotor.ie apm in nu. Where he anveilled his parents tombstone lied he fleed mcp whilst he was not coming home bcs he wanted a faty salary outside malawi.these munthalika’s were not partrotic enouph to their country.be honest.
A NGWAZI IFE ADZUKULU ANU TIKUVUTIKADI,KUNAKAKHALA KUTI AMABWERELA TIKANAKUVOTERANI CHIFUKWA PANO SIZILI BWINO,YOU GO TO A SHOP U FIND THE PRICES HAVE GONE UP NEXT DAY YOU SEE A DIFFERENT PRICE,A NAGWAZI TIKUVUTIKA IFE ANA ANU MAKA ULOVA,KALE LIJA ANA MUMAPEZERA CHOCHITA ENA AMAPITA KU POLICE,KU ARMY ENA KU MYP KOMA MOSAKONDERA NGATI LEROMU,AKUPITA KU POLICE NDI A MULAKHO KU ARMY ANA OTENGEDWA PA GROUND PANJIRA AKUWASITSA KULOWETSAMO AMULAKHO,ANA ATHU MAKA CHIGAWO CHAPAKATI PANO NDI MALOVA,MZIMU WANU UWUTSE MUNTENDERE
Mama C. Kadzamira ndi amene watiyankhulira bwino pa Times TV pa nkhani ya Kamuzu. Amene anaonera akhoza kundichitira umboni momwe anafotokozera momwe dziko la Malawi limagwiririra ntchito za chitukuko komanso za maphunziro. Anapereka chitsanzo cha Kamuzu College of Nursing kuti ana a sukulu pa lunch/supper amakhala ali wempha wempha kunka napita koyang’ana chakudya pomwe kale aliyense akapita ku University amakhala moyo osangalala chifukwa chakudya chimaphikidwa pompo ndiye sukulu imayenda mwa myaaaa popanda mavuto but look at these days ana akuchita rent m’makwalalamu do you think angadzagwire ntchito molimbika atazunzikira maphunziro. Aboma takaonaninso m’mapolicy anu a ma university ndi ma college… Read more »
Kamuzu still stands a HERO OF MALAWI
Pathetic journalism
Apm resign please ulibe mzeru zoyendetsera dziko
APM usatipusitse iwe, kodi 2006 umanena kuti federalism is the way for ensuring equal distribution of national worth.
munthu anawononga dziko lathu ndi ameneyu, foreigner ngati uyu kutilamula nkumatiphanso, mzimu wamatenje, mzimu wasangala, mzimu wachiwanga, mzimu wagadama, mzimu wa silombela, mzimu wa chisiza, mzimu wamuwalo aaah ndi muziti anali munthu wabwino, sizoonah.
Inu a Jona, sikwanu ku Malawi, a chitsiru inu eti! Pitilizani kukamba zokhutazo muone. Tikubwezerani kwanu ku Mozambique. You must appreciate that we are accomodating you idiot – so don’t come with rubbish like that about our presidents. Kwanu komweko! Shit!
Na pa ma prices analibe mzake. All the shops even in the villages were selling things at reasonable and same price. Amayendera from nsanje to chitipa making sure that all is in place and pple are not cheated. Kunenanso za security analibe mzake, lifukulidwe stella maris dam! kkk koma chimanyansa ndi ukapolo, ndi mnyumba mwako momwe!
thats true people were disciplined enough. U see nowadays there is alot of childish even our politicians they are busy castigating each other no time for development issues. Look newly improyed teachers they are not employed up to date since may. Is the Govt serious?