Email a copy of 'Archbishop Msusa urges Catholic women to be agents of evangelisation' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Archbishop Msusa urges Catholic women to be agents of evangelisation' to a friend
Blantyre based Super League side Premier Bet Wizard FC is hunting for a new and well qualified Coach as one...
I thought the Catholic church does not want us, as women, to stand on the pulpit and preach – what type of evangelism is Archbishop Msusa talking about? Let him continue to propagating the perils of patriarchy on which the church survives on – of priests and ‘men’ having a greater role than women. As a Catholic, I am not interested in evangelising because of the church’s attitude toward women.
INU MAYI MNZANGA (A NACHI), ndiganiza kuti tanthauzo la EVANGELISATION simutha kulimvetsa bwino. Zikanakhala KUTI tanthauzo lake lagona poima pagome nkumalalika bwenzi tikunena kuti mumpingo mwathu azibambo (azimuna athu) akulephera chifukwa ngakhale iwo ali ololedwa kuima pagome sionse amaimapo ndipo sionse angathe kulalika mawu a Mulungu poima pagome. Chimodzimodzinso ife amai NGAKHALE mpingo utatilola kuima pagome sitonse tikanakhala NDI mwayi olalika. Kulalika mthenga wabwino (EVANGELISATION) sikuima paguwa pokha aim dipole NDI mphatso. NGATI tikulephera kuyendetsa moyo wathu NGATI azimayi NGAKHALE atatipatsa mwayi woima pagome malaliko athu adzakhala opanda tanthauzo. Kodi ngati tikulephera kulalika kudzera m’ntchito zathu ndiye tingathe kutembenuza anthu… Read more »