Email a copy of 'Blantyre gives Chilima warm reception: UTM promises transformation in townships' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Blantyre gives Chilima warm reception: UTM promises transformation in townships' to a friend
Minister of Natural Resources, Energy and Mining, Aggrey Masi has said the Malawi Rural Electrification Program (MAREP) which is in...
Chilima is going to win elections with landslide on May 21 .Take it or leave it.
Ulemu wanu big mubwere kwathu mudzatenge vote yanu musunge nokha inganditayike
I must say this young man is clearly a very hard worker, i like his work ethic.
1. DPP 2. MCP 3. UTM 4. UDF
Ankatelo atupele mu 2014. Mapeto make analitu number 3. Nanga tiziti kaliati mu boma lero? Tikuziwa ndipo tikuona a bishop awo kupanga zotheka kuti atenge boma poti ndi mkatolika. Asilamu akungopenya, ccap ili phee. Dikilani 21 may.
Milo nvuto ndinu dala. We are campaigning as Malawians not Catholics or Moslems
Whistle stop tour??????
KOMA NGATI WAPEZA MANKHWALA CHILIMA ACHIKOKA WAPEZA AMPHAMVU MWANAYU AKUNDIOPSA
E koma miseu ya mma township. Pa Manja apa Dossi wakhalapo koma anyamata a kwa manje kukoza polowera manja townsgip ndi mbale ya cipepeso. Timaesa azakozapo kuti aziyendera bwino ndi galimoto ya misonkho athu.
Go go go saulos
He has my vote
Apapa Abusa u president ayamba kuuonela Patali, unawayandikila koma ndamva die hard wa Congress akunenetsa kuti uhmmm I like MCP but Chilima must lead and will give him my vote. We dont know how many are thinking like this guy. God bless Malawi
Amalume………… Mabodza chonchi??????????????
Lies a true MCP member can never vote for mbava yayikulu yomwe inathandizira DPP kuwina 2014 forget it.