Email a copy of 'Bullets confirm intercity soccer Bonanza participation' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets confirm intercity soccer Bonanza participation' to a friend
Football Association of Malawi has released the venues of 2015 Carlsberg Cup semi-finals involving Big Bullets, Silver Strikers, Mighty Be...
pi pi pi pi maule adutse
Try other players don’t worry about losing.
dont worry bullets fans as players we shall play this bonanza.
BB MOTO KUTI BUUUU
Inu mabanker osasekerera aliyense.2mili ibwerere Ku RBM.Silver!!Silver!! Silver!!!!!!!.
adafa solder whatmore galu osaka?
BULLETS TIMADYA MA BONANZA OTHILA SILVER, CIVO KUMWERA BLUE EAGLES…….Maule woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
Kodi ku Bullets ku ndi zampira kapena business tsopano,inu nomwe mwakhala mukuyankhula kuti ma player atopa.koma lero mukuti wa ku Lilongwe ku bonaza yachani?
mukufunatu ndalama za nthumba mwanutu osati zothandizira team aii..KELVIN MOYO and RAHIM mwakhala mukuyankhula za kutopa kwa ma player yet lero mukuti team ikupita ku lilongwe zoona zimenzo ma player si zitsulotu ai they need rest.mistake imene mukupangayi muzaikumbukira pa tsogolo(INUSO A FAM KODI PA SEASON KUZIKHALA MA BONAZA ANGATI,ARE WE SERIOUS GUYZ)
2 million only
Point of collection, Civo vs Silver and Blue Eagles vs Bullets. Not lyk the way u wrote there..!