Email a copy of 'Bullets players now focused for ‘more glory’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets players now focused for ‘more glory’' to a friend
Malawi Congress Party (MCP) has refused to apologize for its critical comments on President Peter Mutharika on his UN trip....
Mwaitha kwabasi maplayer bcoz amangofuna kukolora pamene sanalime. shame to u big fish(masapota)
Dzikomo ma prayers we love u all Guys .
Thus Hw The Peoples Tim Iz
Bullets players need to be commended. You are Champions.Donnot be disturbed by these opportunistic supporters.
Ife timadabwa kuti kodi chifukwa chake mumalimbilana MAUDINDO. Tamagwirani ntchito inu ma supporters kuti muzithandiza team OSATI kudyera Maplayers.
Zikomo Ma PLAYERS kuti mwaonettsa kulimba mtima osamawaopa masopota samenya Mpira. MUMABVUTIKA NOKHA NDI TRAINING KOMANSO PA GAME.
Ok, let me c outside. # feels gud to be back in love!
zilibwino
ONSE OKHUDZIDWA NDI CASH GATE KU STADIUM ASAPASIKESO MPATA KUYENDETSA TIMUYI MWANJIRA INA ILIYONSE.
MBAVA ZONSE KWAWO!!!!!!!
Anthu osakonda timu ngati awa sakufunika
Abale mwanyany kutola khobwe. Team ilibe ndalama. Player monse wayambira kukhetsa thukuta phindu lake osaoneka. Alipo ena amapita ku stadium game iliyonse koma kuwafufuza kuti mpira adaonera liti simulipeza. Amangopitila kukaba mma gate basi. Anthu onyansa inu. Kubwezeretsa mpira pansi basi. Stupid!
Basi anthu kumangozolowera kuba malo muwona umphawi wa Team yathu kuti ulibwanji mukufunanso kuyibwezeretsa pansi team otero akapezeka olakwa achoke.