ayankhula bwanji chizungu ngatiali mpakamwa poyankhulitra chizungu…zaboza bas
fuziyawo
8 years ago
Is this newsworthy? Mister Muheya we already know about this..why recycle stories.
There are alot of better sports stories to write… i guess you must be suffering from xmas and new year’s hangover
Kwaderanji tiyambe mijedo
8 years ago
Guys let him claim his outstandings balances, there’s nobody who works for Mahara. And it was so bekoz of Maullets financial muscles. Karry on Kananji Hey !
Nyenyezi
8 years ago
Ngongole ya Kananji ndiye kuiika pa front page chifukwa ndi ya Bullets, ngongole zonse zili ndi a nomazo simunanene bwanji nthawi yonseyi kungoika ngati related stories? Zokondera basi unethical reporting on Nyasa Times.
‘Bullets yet to pay me’ wayankhula ndi kananjiyo chizungu chimenechi kapena mukumuika mawu mkamwa
AKIJA
8 years ago
Waona chithumba chili ku Bullets ha ha kananji
Ndaipalero
8 years ago
Kkkkkkkkk kananji tiona kumene ulowere ndi kupanda xool kwakoko neba akulavula ulibe certificate iwe bwerani mudzatenge mwina mupite ku xool maulle ndi deal basi
ayankhula bwanji chizungu ngatiali mpakamwa poyankhulitra chizungu…zaboza bas
Is this newsworthy? Mister Muheya we already know about this..why recycle stories.
There are alot of better sports stories to write… i guess you must be suffering from xmas and new year’s hangover
Guys let him claim his outstandings balances, there’s nobody who works for Mahara. And it was so bekoz of Maullets financial muscles. Karry on Kananji Hey !
Ngongole ya Kananji ndiye kuiika pa front page chifukwa ndi ya Bullets, ngongole zonse zili ndi a nomazo simunanene bwanji nthawi yonseyi kungoika ngati related stories? Zokondera basi unethical reporting on Nyasa Times.
Waona maule apeza chithumba wayambapo kuwawata
Chifukwa chot za bullets zalowa”?
Ndaipalero, that’s out of context. Appreciate facts as they are.