Email a copy of 'Bullets to discipline Kondowe and Nyirenda' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets to discipline Kondowe and Nyirenda' to a friend
Eleven United Democratic Front (UDF) members of Parliament (MPs) who moved to the government benches in Parliament who gone to...
Zimachitika munthu salephera kulakwa.koma asaonjeze
do these players think they are bigger than The People Team itself? Never. kachilango pang’ono basi apasidwe azazolowera
Let us call a spade aspade. Fisher is fast becoming outdated, he is way past his prime but only his name is making him cling to this bullets team. He used to be good, but that is about three or four seasons ago. Time is gone when names used to play football, pano the work is done on the ground. Passenger players like him will only burden the other 10 able players in the field of play. He just need to let it go….. George Nyirenda is just an average player. There is nothing special about him (apart from the… Read more »
Nzika uyambe kuiya akazi ako ukadawanva kukoma, why kuti munthu asiye pomwe amapezera capital yake. Nanje bwanji
vachamba ivi visiyeni!!!!!
iwe rahim ishmael, zoti uzilimbana ndi ma players like Fischer sizikuthandiza, ndipo uyenera kuzindikira kuti Fischer is our living legend. Zimene mukupangazo zomakhazika Fischer panja zikubwezeretsa mpira mbuyo. Ndipo aliyense akuziwa kuti Fischer amatha ndipo zomwe mukupangazo zikubwererani.
@ Fischer-Kulibwino kusiya zinthu zikadakoma osati muyambe mwakangana ndi anthu.kukanakhala kwabwino kuti anthu adzakukumbukireni ndi zabwino zokhazokha osati zimene mwayambazo.@ George ukutionjeza kwambiri.popita ku Zim unapanga chipongwe pano takulandira wayambanso zachamba zakozo.Watch out ur not bigger than the Team.