Positive move for Malawi football.Lots of goodies for Chiukepo.
Miilion Mawa
8 years ago
Chalembedwa apa ndi chizungu muthokoza bwanji a Madukawo ngati kuti Chiukepoyo watengedwa kale. Mau akuti (earmark). Mwayiwala kuti pompano msilikali wina anali ku john konko nkumanena kuti wachita bwino koma pano bwa nkhani ndi yomweyo ma trials anali bwino koma kungoti………….

Am wishing u all the best.God bless u
I wish Chiukepo all the best. Thanks Mr. Maduka for promoting home talent. Takunyadilani.
I jst wish him all the best