E-Mail 'Chakwera storms Malawi  Electoral Commission: Opposition leader meets chief pollster' To A Friend

Email a copy of 'Chakwera storms Malawi  Electoral Commission: Opposition leader meets chief pollster' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
newest oldest most voted
Notify of
Tizanka
Guest
Tizanka

If one is failing to mobilise his supporters to go and vote then how are you going to mobilise this country towards the right direction?

chatsika
Guest
chatsika

Munthu wa mtundu wanji osiya kutumikira Nkhosa za Mulungu ndi kumatumikira za mdziko lapansi. Wakumwambayo wakana basi mpando wa u Presdent siudzauona. Unatukwan Mulungu iwe. Mundipatsireko Moni kwa Mayi Ntaba a ku Lilongwe paja ndinamva kuti man of god amacheza nawo kwambiri .

Truth pains
Guest
Truth pains

Chakwera, that’s misleading the people. The best way would be to give reasons why people did not go to register. Even if the centres reopen do you assume.e that they will go and register? Can people be forced to register? My interest would be why they did not register when the centres we’re open? Let’s address that problem

Symon Tshaka
Guest

All I want is that rubbish (mutharika) to leave the office. We all aware that Mr Chakwera and his mcp can win or they will win but this DPP will rob him again like before.

mtete
Guest

The fact that MEC started the registration in MCP strongholds and deliberately frustrated the process in these areas is concrete proof that the organization is out to help rig the election in favour of DPP.

DPP can do it since it has lots of money squeezed from, among other sources, dubious contracts such as the Police Food Supply Contract. They can corrupt all MEC members with millions of kwacha several times over.

DOBO
Guest
DOBO

Mabvuto a registration abwera chifukwa choti a MEC kumayambiriro ankanena kuti National Id idzagwiratsidwa ntchito pobvota.Izi zimakambidwa koyambirira kuja id registration isansyambike.Ndipo ngati mungakumbuke panali mtsutso waukulu ndipo ena amati a MEC mogwirizana ndi DPP akukozekera kudzabera chisankho.Pamene idathera nkhani imene ija mpakana pano anthu ambiri sakudziwa kuti nkhani imene idathera pati.Tsopano chipwilikiti chadza nkuti NRB ndi aMEC akuyendera limodzi.Pamepo!!!!.Moti anthu ambiri akuganiza kuti National id idzagwiritsidwa ntchito pokavota.Pangani kafukufuku zimene ndikunenazindizimene zili pa ground.Zifukwa zonse xija akupereka a MECndizolakwika.

Hatton
Guest
Hatton

Yes Leader of Opposition but you forgot to tell MEC that they should not allow any political leader, including the Leader of opposition, to intimidate MEC officials. Ndi tulo teniteni kuyembekezera a MEC kuti azikasaka anthu m’midzi kuti akalembetse. Ngati anthu sanakalembetse limelo ndi vuto la anthu onse a ndale a m’dela lokhuzidwalo. Akulu siyani kuopsyeza anthu ogwira ntchito Ku MEC.

China
Guest
China

Mbudzi iyi apange campaign yowauza ma supporters awo akalembetse.UTM woyee

Kasumbadedza
Guest
Kasumbadedza

Mwayamba kale kutukwana musanakhazikitse ndi kagulu kanuko? Ndie muyembekezera anthu make ati oti adzakuvotereni? Mwagawana kachipani inu multi nd1teth of voters mwamba kutukwana?

malawi
Guest
malawi

Dear mayi Jane Ansah.

Do u want to hold free and fair elections? Mayi chonde chonde chonde samalani dziko.lathu. we are not going to allow any rigging. we are ready only for fair elections. we r 100000000% watching. we will never allow kuba any more.

Malawi is on a verge of conflict if u don’t do right things coz we will not allow cadets to castigate n torment us.

sck
Guest
sck

GreatLeader. man mumayitha. anthu akubawa osawasiya. DPP A nd DPP B. anabera ma vote anthu amenewa in 2014..