Email a copy of 'Chakwera tones down criticism of Mutharika: 'MCP move on to rebuild'' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

84 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Magaseni
Magaseni
9 years ago

Kodi mtumikiyu bwanji ndimukumbutse za Yona, waiwala Ninive? waganiza mochedwa zomanganso MCP, ndikumangolimbana ndi DPP, kodi mtumiki uyu ndiye kuti salosera? osadziwa zoyenera kuchita nsanga? Tamverani GOGO wanu zimene walankhula zanzerutu ngakhale nzerunzo zabwera kuukulu.

dennis jovi
9 years ago

i will hate mcp 4the rest of my lyf anthu ankhaza ngati inu, zoti muzalamulanso dzikoli 4get.

E Chafuwa
E Chafuwa
9 years ago

Mtumiki wa Mulungu azitero Keep it up

David Maseko
David Maseko
9 years ago

Dr L Chakwera, MCP President; Be applauded for the comments for urging the MCP followers to bury the past and focus on the improvement of Malawi economic condition for the good of Malawians citizens.

The wisdom lacked by many party followers is that of not putting interest on the have-nots.
You are the man of God therefore should fulfil God’s love on Malawian nation. Don’t bend down your Christian morale because of unruly followers.

Keep that spirit burning in you always. God bless you always.

Alfred Munduwabo
Alfred Munduwabo
9 years ago

Please , Dr Rev Chakwera won the presidential elections but DPP destroyed the evidence by using Dausi and DPP crooks by playing around with ballot boxes.

I am just feeling sorry for our president Dr Rev Chakwera declaring of supporting the government which all donors are refusing to support.

nkhakamila
nkhakamila
9 years ago

LOMWEEEEEEEEE.THE GREAT.ZILIMBANANI WE ARE COMING 2019,TABEREKANANSO KWAMBIRI MULIMBE KUTI MUZAWINE CHIFUKWA ANTHUFE TILIPO AND TIKAZAPANGA AMAGAMATION NDI UDF KAYAAAAA……DZIKO ILI NDI LA AYAO NDI ALOMWE BASI.VOMEREZANI!
\

Mbwiye
Mbwiye
9 years ago

As long as Lazalo Chakwera still believes that his vote was stolen, I can not respect him. I expected him to concede defeat without crying like a baby or to produce evidence in court that his vote was stolen. He would have produced precedence that would assist law students at our Universities. For him to say that he has forgiven is an insult to my intelligence. My question would be whom has he forgiven? What evidence has he got that his vote was stolen. Did people from the North vote for him? What about people from the South? Can you… Read more »

Ngoni10
9 years ago

ndikuuzeni mpc followers ngati Simudzasiya kunena kuti dpp ndi chipani cha alomwe musayembekeze kuzalowa mboma chifukwa malawi si alomwe kapena alomwe thewayyouaredoing mitunduina ya central region wont vote for you these parties are for malawian period

Moyenda Chisale
9 years ago

Iwe ukutchula Ambuye adzatsogolella a0 Chakwela kuTi awine chonsecho ukuneena zoti alomwe nDi akuba kodi siudziwa Mulungu funsa Chakwela wakoyo amene anauza Mulungu kuti kutumikila za uzimu ndasiya ndipita ku za dziko. Akunamatu ameneyo abwetrere kwa Mulungu. Komanso mukamanyoza mittundu ina mukuona kuti panokha mungawiniitse Chakwerayo onetsani chikondii posayanh’ana mtundu

FCK
FCK
9 years ago

Mtsogoleri okonda dziko lake azitero ndpo tikuyamika chifukwa alomwewa anaba mavoti ndiye poti ndimbava inu imani pachilungamo dzikoli inu moikidwa ndi Ambuye mulamulira ndithu kaya ena anyoza kaya akambirana ndipo inu yendani dziko lonse phunzitsani umodzi ndi mtendere kukhuluprila komanso kusunga mambo ngati mtundu wa a Malawi, chifukwa utsogoleri ngati wanuwu ndi umene wakhala ukusowa mmalawi muno kwa zaka 20 tsopano

Read previous post:
Vote recount bid lacks merit, court rejects DPP’s Mussa

The High Court in Blantyre dismissed  a poll results dispute case for Zomba Central Constituency  in which  Democratic Progressive Party...

Close