Email a copy of 'Chilima excited with UTM progress: Movement leaders go to rural hinterland' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chilima excited with UTM progress: Movement leaders go to rural hinterland' to a friend
Newly refurbished Eastern Region Immigration office in Mangochi is now ready for commissioning, Director General of the Department of Immigration,...
Zidakwa izi. Zimapita kimisonkhano zitaledzera, makamaka Chilima. It;s good Malawians have known this well before they commit their support to these drunkards.
Kwathuku Ana ndamene ananjoya after choimbita dance….ntchito njosayamba..limbikani makosana,mtunda ngwaukuku ndithu..vuto ndi loti anthunu muli pa changu chachikulu..ma results amene mukufuna di nthawi nthawi mmmmm sizikigwirana ndithu..koma kuyesa nkwabwino ndithu all the beat..
Asasamba awa pa ndale! nsanja ndikukhala mpando eti? frustrated asasamba kkkkkkkk
Crooked Party why registering an abbreviation.Kuyamba kupomboneza Registrar of Political Parties ndiye ife atiputsitsa zedi.
We should all thank Peter Mutharika’s sloppiness which ushered UTM. Whatever happens with UTM come next year May, Malawians can only be winners. The entry of UTM into the fray has brought about real politics in Malawi which, I guess MCP, would have been unable to do. DPP arrogance is waning as it can see that there is a new sheriff in town ready to eat its lunch. They can ignore UTM at its peril. DPP and MCP will have to up their ante.
UtM woyee all civil servant , vendor, farmers are behind you . do no let us down
Kuzikwata ndi chalatu uku. Okay, go ahead. Kulota saletsana.
Mapazi ako gulukunyinda
koma ine iyayi. zandale ayi. so don’t generalise pliz
Surely where is Usi’s audience?
Ife phee kudikira chimbale cha ‘Atibela’. Paja ma UTM ndi MCP mwati Sikudzakhala kubela eti? Mwina chimbalechi sichidzatuluka kapena mudzatulutsa choti ‘Taludza tokha’ kkkkk. Tiye nazoni kuyetsetsa kuwonetsa ngati zikuyenda pomwe zoona ndi zoti ku UTM zasokonekera….moto wa mapesi uja wazima kkkk. Mwayambanso kukanganira mbwelera za mfundo; Tambala wakuda akuti Namalegeni akuba mfundo naye Namalegeni akuti tambala akukamba mfundo zake hahaha…phada wa ana ndithu.Mudzichedwa nd kuloza mfundo anzanu akuloza zomwe achita kkkkkkk ziliko chaka chino.
Looking at the partronage in these so called meetings ,you can tell that penetrating rural areas is not a simple task .Even nyasatimes guyz can not give pictures of such meetings.Preparing to be in opposition benches come may 2019 .Tiziwona ife wathu tinasankha kale olo mutamenya kampu panyumba panga sizingaphule kalikonse.
Very right to convince the rurals eish it’s an ant hill,especially when the government you are despising is doing a lot of development.
Moto wa mapesi indeed. You think Malawians are so stupid as to follow the frastrated group of politicians
Fortunately anthu adziwa kuti this is acamp of drunkards, whorls and frustrated idiots.