Email a copy of 'DPP, MCP fight at funeral in Kasungu: Ntaba evacuated to safety' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP, MCP fight at funeral in Kasungu: Ntaba evacuated to safety' to a friend
First Lady Gertrude Mutharika has encouraged all women in the country to strive in upgrading their education levels. She said...
my party at its best
opposition kuthibula ruling hehedeee.
Kodi mesa muti inu alomwe kasungu nkuchipinda kwanu ?Ma tenants mulipo angati munya muona.
Komaso tiwauze a Malawi kuti sizoona kuti abanja LA kwa Snr Chief Lukwa akudzudzula boma kamba ka zomwe zachitika ku Malirozo nkhani ndi yakuti abanja akudzudzula otsutsa boma kama ka Ziwawa.
Tiyeni tiphuzire kulemekeza Maliro izi zopanga ndale pamwambo wachichewa sizimaloledwa
Nkhani ili apa ndiyakuti tiyeni tilore kuti chilungamo chiyende ngati madzi padalakwika kuti Hon Nkhata adalanda Mkuzamawu kwa Master of ceremony. Izi zomapanga ndale pamaliro zikanatha.
Malawians why wasting your precious time talking about Ntaba.This man has no value in Malawi’s political establishment apart from BEING THE KING OF OPPORTUNISM in the history of our country.The Party in which he is today,explains a lot and march his satanic ideals.This is the man who is now strongly suspected being the murderer of the founder and first President of the MALAWI CONFUSIONIST PARTY hereinafter the (MCP),Mr.Orton Edgar Ching’oli Chirwa QC.In general,Ntaba is a dead soul you never trust him when it comes to KWACHAS,this is the man who has no vision like the Party he is serving today… Read more »
Ndemanga za achipeta ziri zagule wamkulu basi….simudzalamuliranso dziko lino agalu inu. Munatikwana.
Chipani cha dhiphiphi chatha taonani A Ntaba amakatani tele ku Kasungu ajiwako i
Zautsiru zanuzo a dpp muzikapangira ku maliro a ku thyolo, mulanje kapena phalombe. Anthu ochititsa manyazi inu. Simudziwa kuyendetsa dziko mthawi ya zipani zambiri. A malawi anasankha zipani zambiri kuti dziko liziyenda bwino. Koma inu zamanyazi.
DPP zitsiru za anthu.