First Lady’s aide booted out of State House
Malawi Government has a special aide to the First Lady Phillomina Kasambwe in less than six months of her employment, State House chief of staff Peter Mukhito has confirmed.

Mukhito, however, said Kasambwe will not be jobless as she will be redeployed to other duties within the civil service.
He disclosed that Kasambwe’s next assignment is at Airport Development Limited (ADL).
Kasambwe, who once served Chiradzulu Central as a Democratic Progressive Party (DPP) Member of Parliament, was the First Lady’s special assistant.
Meanwhile, Mukhito also confirmed the story earlier posted on Nyasa Times that State House press secretary Fred Ndala, journalist by profession, has been sent packing.
He said it was true that Mdala has been given the sack at State House and that he will be redeployed like Kasambwe.
Follow and Subscribe Nyasa TV :
God save Malawi from bad behaviours
Ntchafu kapena kantchafu? Shupiti woman, kuonekanso kuti makomedwe mulibemo.
Please chonde azimai dzisamalirani kuvala nanga mpaka chonchi tchafu?
THIS IS WHAT I SAID PREVIUOSLY, STILL THE GAME IS NOT OVER, WAIT MORE ARE IN THE RING AND OTHER SEALED BOXES ARE NOT OPENED YET. MORE FIRE ON THE WAY.
Amina , muwonesese bwino fotoi ! Mai wa zawhite wakhala pampando , manja ,manja wakoleka pa mpando . Sinchafu ai. Onesesani bwino bwino
NO 41, imeneyo ndi ntchafu. Kodi ndani akudziwa mwiniwake wa ntchafuyo? mwaiona bwanji?
away from the story is the person sitting next to the first lady wearing anything below her buttocks? Pliz whoever has good eyes let me know. Akukhala ngati sanavale chili chonsetu. kikiki! Kunali kuti kumeneko?
Chitukuko pa Malawi, ntcha izo m’boma, imeneyo si Cash Gate iyayi ndi Cash Man!
tyme-tyme
Uthenga wanga kwa President wadziko Lino ndi inu nonse andale. Would you please leave the professional jobs to professionals and let politicians do their politics. It is demoralizing to professionals. Zoona ma cadet azikhala akulamulira munthu woti akuiziwa ntchito do you expect kuti zinthu zingayende? Ngati dziko Lino lisakitukuka nkhani Ina ikuvuta ndi imeneyi. Mukumatenga ma cadet kumawapasa maudindo mma institutions aboma cholinga azibamo. Bwanji simumakawasiya ku defense force or police mumaopa chani. Ndichimozimozi ndi MRA sangazikwanise zinthuzi ziwauikani malo oyenera
Politicians!
Kódí wakhala pa mpando winayo ndani? Nanga chikuonekacho ndi chani kodi? Ntchafu kapena? Kkkkk….. Ndithandizeni anzanga
Malawians learn to be civilised, this is in US, she might be an American, British, Tanzanian, Zambian. Mind your own chitenje clad woman there
Typical of political positions!Nothing strange
Tien timange malawi osati kupwasula
Kodi mzimayi winayu mavvalidwe amenewa kapena ndi chani?
Muli inu mungamve bwanj? Mumayakhura zotumbwa kma simutha kupeleka maganizo abwino khani kunyoza bas ali mwana wanu mungamve bwanji? Muziyakhula zomanga kt enawo obwerawo….,,
Good people, help me to see, what is the lady sitting next to the first lady wearing? Eiisiiih fashion….?????
Getrude watulukira mochedwa kuti amwene Peter amadyanso Kasambwe….koma akanatani poti Kasambweyo ngokongola wasiyana ndi mbavayo…nkhope zonkira kupusi zija
N’kutheka kuti First Lady amaona APM akuphethila kwambiri akaona Philomena.
Transferring a problem!!? What is the problem with these clueless DPP leades?
Mukufuna kuika abale anu ena. Opusa inu. Chupiti.
Phillomena ndi wa boo Mwina nkutheka wasokoneza kumpanda.
Try to be a right people guys
Bwezani ndalama inu pamodzi ndi manganya wanuyo pamisundu pinu aagalu inu
Kutenga ADL ngati ya state houseeee kapena kuti ya Mai anu????Redeployed kutiko kumene apite???Apititseni kumudzi kwanu uko ku Thyolo stupid,you failing kubweza ndalama ku NAC kutisokosa ndi zauchitsiru.Muona pa 13 jan. apa.
Palibe pepani zavuta basi
Ndalama dzimapita ku ndalama zimzake. Post yomwe amuikayo pali ma graduate omwe akusowa ntchito omwe amayenera post yomweyo. Koma basi ndale.
Getu achoka Liti?….za NAC übwenze iweeeee
I wonder that these people you are now booting out from state house were picked from somewhere outside the civil service.
Now that you have booted them out you say you are going to redeploy them. To where if I may ask?. Why not let them go back where they were before you picked them. Was it a means of bringing them into the main stream civil service by the back door?
zayambika zanu izooo.
So you want to send Kasambwe to ADL, I think you put ADL away from politics.
Kabwezeni ndalanazo ku NAC apumbwa inu.
sapepesa kkkkkk
This is not sacking but rather chopping off ina de tchopa style. Mukhito ndi mbuli basi. He is an ex-brutal policeman with blood all over his hands.
Dziko liri m’mnja mwa Alhomwe. Anzawo akuberekera ma Laptop bag iwo amaberekera amphaka akufa akuti gule wa tchopa.
Normal kungoti mabodza achuluka ku state house bola kuklemba kwinako koma it’s normal for any job to be kicked out
The normal practice is that personal aids/assistants are redeployed else where in the civil service if they were drawn from the civil service to become assistants. You don’t redeploy them if they weren’t civil servants s they are just appointed on preference of the politician to be served and don’t go through the civil service hiring procedure. The redeployment of the two into civil service is unprocedural and uncalled for. Is it just a way of giving permanent jobs without following the established procedures?
CZ ndiye ku State House mwazazakotu
They are going to be redeployed? In reality what this means that is that they are being imposed on another organization where there services are not required at all and will therefore be drawing almost free salaries. Meanwhile State House will replace them and in the process increasing the number of public servants at a time when the same is preaching about reforms. By the way it seems as if it was mostly ex MP’s from the southern region who were given jobs after flopping at the polls.
AKUTI AMADYESA KATUNDU KWA BIG MAN
Mukhiti sapepesa
If not perfoming why keeping her? When in Rome do what the romans do. Try others who may perform madam Apm.
Sitimalowela za Alhomwe Ife. Thanani nokha kumeneko. Mwachulukitsa mpaka ma driver mbweeeee osowa chochita. Ena a kuti tinabwela ndi Chisale ena Ben kodi kuli ntchitotu
Kkkkkkk
Thanks for the information. It clearly shows that the employees being redeployed did not meet the required work ethos.
Zanu izo
There is a very big difference between sacking and redeployment Going by the story this is redeployment and not sacking
Kaya muchita motani? kaya mudzi chekacheka ife tikufuna ulamulilo olongosoka. Emulate malemu mayi TEMBO am happy u were there and mwadzimvela nokha.Tayeselankoni chonde, makani ndi momwe muma onekela sizigwilizana.
Izi ziri pachiweniweni wa Mlakho, ife zisatikhuze! Sankhani mlomwe wina. Getu sangakhale ndi aide wa nzeru kwa nthawi yaitali, ndiyeno mukasankha wina muonenetsetse kuti akhale wopepererako ngati a Getu wo.
ALOMWEALOMWE
Mesa mudawalemba nokha ndiye ife mukutiuza chifukwa chani, mukito sangapepese iyayi! Muona mutsegulira skool zanuzo nokha ife sitipeleka Education Freedom yanuyo,!!. Kapasula: kapasula ndiye kuti chani? Eh!!! Sankatsutsika mukhito pali mbuyake uja inu musayembekezele kumuuza zochita and think akunvelani ata!! expect more sackings asadati, ifeyo osamatisokonsela ndizamanyi zimenezo ayi!!.
Kaya zanu izo, mavotavota…
That is normal
Mwina anawapempha kuti abweze ndalamazo, ndiye paja ka mtundu kameneka ndi arrogance, eish.
Booting ppl out of state house z normal in piolitics
mukhitho sopano wajailatu….