Email a copy of 'High Court dismiss MCP faction on convention case: Chidzanja dissapointed' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'High Court dismiss MCP faction on convention case: Chidzanja dissapointed' to a friend
Transglobe Produce Exports Limited Directors appeared before the joint parliamentary committee probing maize acquisition from Zambia where they categorically denied...
nde muganize akakhala ca buno ngati timbalame ta pa lilangwe. azimai otopa awa. awa a MC anangotengako nthenda basi. uyu nkulandilako ma 40 plots kuwasiila stam NAMASALA. mciuno anthu a ndale. zao nzimodzi.
galu oba cimangayu mwaiwala anakwwiitsana ndi nzimai ku Ethiopia/kenya ,atabhuka hotel nzimai anankana. mbala imeneyi zikumuyabwa ndalama. eti kunyasa cimunthu cake. mpake lelo anthu angobisalila mmipala, koma ife tikudziwa.kkk kkkkkkkkkknde Catinkha wawadzoka heavy anthu awatu. kkkkkkkk
Chatinkha, aaaaaaaaaaaaaaaa,,, koma inu
My concern is on the lady leading the group, Mama Chatinkha Chidzanja. She is using the group for her own personal agenda. Her loyalty to the party has always been questionable to me. She wears two colours; that of MCP during day and DPP during night. This lady had been allocated and given over 40 plots at Nalikule along Salima Road by the then DDP diehard CEO of Lilongwe a Mr Mmangisa who was always the MC on all Late Bingu’s occasions. Who among the opposition diehards and MCP in particular can be given such a chunk of land by… Read more »
MCP dzulo ku khoti, lero ku khotI, MAWA KU KHOTI. aPO AYI PA Zodiak. what a party?
tchaya tiweruke zopusa bas
Lawyer worth his salt & caring for his reputation not just after a quick buck would’ve surely told the claimants to go find another legal rep coz apapa ambuye aNamasala mumati mukupita ku court to win? Shame on u Namasala. Of course bola wapeza ya mchere koma ineyo ndikuzisaka kwakoko can’t trust u to represent me ntafuna lawyer coz iweyo za reputation yako ulibe nazo filimu bola bongo basi
Is this not Chatinkha Chidzanja Nkhoma who was on TVM a decade or so ago telling the Nation that she was HIV positive. Kindly remind me in case this is a different one. She also confessed that she is njinga.
MCP & Chakwera are Mighty.So if you know that you have a mental problem,don’t dare to tamper around with it.You thought you will become heroes but alas!you zeros.What a Shame!Now what next?
Ngati akufuna ayambitse chawo chipani koma ngati sangathe abwere tigwirizane pakugwira ntchito za chipani chathu chokondedwa potsogozedwa ndi Dr Razarus Chakwera ngati president wa MCP.
INE PA CHIDZANJA SINDINGATOTE LOKO PANG’ONO! KKK TIMIYENDO NGATI TA MBALAME YA TIMBA>