Email a copy of 'Hooliganism raises its ugly head in basketball: Cezobal metes out stiff punishments' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Hooliganism raises its ugly head in basketball: Cezobal metes out stiff punishments' to a friend
Members of Multi-Party Constituency Committee (MPCC) for Dowa Central has been lauded for the effort it is doing in uniting...
Iwe ukuti ndiwe ladies kaya ndani zomwe tikunena apazi ndizowona zokhazokha ndi wa ndewu ndi ku za ndale zomwe. mufufuze bwinobwino. Ma business ukunenawo amatakata ndi Lutepo. Sikuti ndi nsanje ayi. Nsanje ibwerera pati ngati ali ndi kanthu iyeyu
Mhehehe thats what happens when we have so many brainless bouncers in one team… China nchina Adrian Kaliu zamuphonya pati? Iye ndewu samatha?
Mmmmh
Iwe chindere n teacher kambani za mzeru apa. These guys r stars n they hav achieved alot as players successful outside basketball too. Ine I follow Cezobal kwambiri n many chindere u thot Tendai akukwatira now unagwa nawo ,coz ndiwe mkazi wa grandpas in town. Let him enjoy bball with happy marriage life. Good luck Tendai, I don’t know much about this verdict so I can’t comment.
A teacher heheh mpaka JB zomwezi? Y do u savages connect anything to politics? Eh tamakulani inu.
Cezobal committee I jus hop ur verdict is fair.
Tendai Banda amchita bwino as he uses basketball kupanga zibwenzi. Tatopa naye yet he is married . concentrate on your marriage
Yes its a mimbulu free league. Ah anawina kokwana Pano amatilemera. Many people in Cezobal don’t want mimbulu n we support you Mr chairman. Congrats.
Dan Zimba ndi mnyamata wake wa Lutepo. He used to be a morale boy wa a Mayi. Ndizosadabwitsa izi. Kunyoza a mayi pali iyeyo ndiye kuti uvulala. No wonder ku Sozobol amangokhalirako ndewu. Good riddance for Sezobol