Email a copy of 'Husband hacked to death by ‘jealous’ wife in Malawi gruesome murder' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

72 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chaiwala H.S.
Chaiwala H.S.
9 years ago

Amayi Kaliya muli kuti? A Seodi White muli kuti? Nanga a Jesse Kabwila muli kuti? Uyunso ndinaiwala Kwataine Marita mulipo? We hear make more comments when men have done something bad on women why don’t you condemn this unbecoming behaviour by this young lady kupha mwamuna ngati apha nkhumba kapena ng’ombe? If it were mkazi waphedwa in such a brutal manner media yonse kunali gwedegwede kodi ziditero? Gender equality mumaifunayo ndi iti? One thing you shud know sizidzatheka kukhala gender equality ayi. Mwamuna sadzatengapo mimba wosatheka mkazi sizidzatheka kupereka mimba kwa mkazi ayi. So zinazi ndi bwino kuazimasulira bwino otherwise… Read more »

Goodson Zimveka
Goodson Zimveka
9 years ago

women r bad

muderanji
muderanji
9 years ago

Zomvesa chisoni amuna onsewa mwina ndi mufti

boid
boid
9 years ago

Tiko, Number 64, the couple was from Ntchisi and went to Nkhata Bay for ntchito ya ”utenant.”

Tiko
Tiko
9 years ago

The lady is only 21 against this man 32. Is this not childish kind of behaviour. Atonga a Bura ndiye yapa chavuta uri?

KUCHITEKETE
KUCHITEKETE
9 years ago

SAMVA ZANZAKE ANAMVA NKHWANGWA ILI MMUTU…..KOMA APA MATHU MWAONJEZA. MUKANANGOSAMUKA NGATI SAMAMVA MWAMUNAYO NDIKUKAKHALA KWANU KWABWINOKO. MUKANAFUNSA MMENE MKAZI NZANU WA “”MESHO” ( WIFE TO KAMOWA) ANACHITILA.ANANGOSAMUKA AND FILED FOR DIVORCE…I CONGRATULATE HER HER AND WISH ALL PRESSED IN THEIR MARRIEGES SHOULD EMULATE SUCH A COMMENDABLE ACTION OSATI MAZUNZO A NDENDE MWAPUTA APAWA!!!!!!!!!

weddington kamanga
9 years ago

Ayi,akanayenela kubwenzerapo chilango cha malemu kamuzu banda chija,wopha mzake nayeso aphedwe.mwina anthu angaphunzire kukhululukilana.zomvesa chisoni kwambiri.

martha
martha
9 years ago

Mulungu atithandize.kumeneko timati kusowa mzimu.mwana wa mwini kumulimbira mtima choncho?Bwanji osangomuleka nawe kutengana ndi amuna ena?satana wakuchenjererani mai.

yeah yeah
yeah yeah
9 years ago

Simunati………… mukhalapana

Kadushu
Kadushu
9 years ago

womens groups please comment

Read previous post:
Nomads staying up, beat Red Lions: Malawi TNM Super League

After a season of so much torment and frustration, and facing the prospect of a relagation, Mighty Wanderers seem to...

Close