Email a copy of 'Injury blow for Malawi skipper Joseph Kamwendo' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Injury blow for Malawi skipper Joseph Kamwendo' to a friend
Malawi Revenue Authority (MRA) beat its first quarter (July to September) revenue collection target by K880 million (US$2 120 482),...
Sopano avulalira mpira wake uti ,kikikikikiki kukhalangatitu wa palachuti batalion ,ati atavala nkepi pa head , kuwufira kumeneko kikikikiki.
sorry
Laugh,Laugh,laugh not so? A Malawian so called professional at TP Mazembe, not even warming the bench there but captain of the FLAMES with very little impact for the team.Isn’t this a pity to expose such mediocre standards of football when depending on such calibre of players? His second coach lamented the loss on travel lags,what? What about Ethiopia?they traveled to Mali and registered a sweet victory there.Algeria also traveled back to their country but with little negative effect on their performance.Stop excuses coaches,you aren’t just good enough for the poor team that needs a well qualified tactician. I feel sorry… Read more »
We r going to mis you mr JK.May god gide you
koma ichi ndichinbuzidi ait kuchipatala chikowona ngati malo osangalalako zalazo ndiye ukumuyimikira ndani ,akuluakulu ichi sichinavulare chikuthawa ma game enawa chikuziwa kale kuti abwantasa anzakeo aluza akale
Inu a Yakunowa dziwani kuti ngakhale pamaliro nsima ndi ndiwo zankhuli zimadyedwa. Kodi tinene kuti anthu alibe chisoni? Munthu ukavulala ndiye kuti basi uzikwiya. Kamwendo ndi player mufune musafune. Player amayenera kukhalako pa bench nthawi zina. Nthawi yolowa umadziwa chochita ndi kusintha game. Malankhulidwe anuwa akuonetserathu kuti mpira simunasewerepo chikhalireni.
even if you get injured, idiot, you are always in civilian during tp mazembe games, when you come here for national duties nde uziwoneka ngati dolo, celebrity, za ziiiiiiiiiii!!!!!!!!!!
a number 1 mumafuna azimvesa chisoni chifukwa ali pa injury???? kkkk anthu enanu mumaganiza bwa? munthu ngati wavulala sizoti nthawi zonse azimvesa chisoni, phychological happiness speeds recoverly ndikuuzeni ngati simuziwa.
Get well soon.
Jack, the Algerians also travelled..to and from malawi and also played….so what r u saying man???? So find another excuse please…..