Email a copy of 'Joyce Banda highlights women challenges at BBC conference' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Joyce Banda highlights women challenges at BBC conference' to a friend
Malawi leading mobile phone operator Airtel has donated a whooping of K6 million to Malawi Queens as they prepare for...
chilungamo chidzadziwika mayi Banda,kuti ndinu wakuba?
Madam, come home pliz Malawians are waiting 4 u to defend yourself on cashgate issues. For sure your bail will not less than 2 billion kwacha.ur mphwiyo has already slapped with 12 mita bail bond. So don’t run away trying to buy sympathy from azungu and black mailling APM.Mutipeza tili konkuno.
Life is not always easy ,it needs patience and perseverance. people people munyenge mavi ya mbewa ndikumwa mikonzo yanu
Pamaso mukamayankhula ngati kuti ndinu abwino,koma eeeeeeyi!!,Sikidzi yeniyeni.Muthu woyipa,tamabwerani kuno tione kuti zidzatha bwanji…..
JB, more fire! the only wise leader Malawi has seen after Kamuzu Banda. Osati zina zija ndi zinazi!!!
amai mukubwera bwino
Koma inu, chitsime chimaoneka kuti chinali chakuya chitaphwa…amayi atangokhala 100 days m’boma ayi ndithu mabanja anayamba kuyenda bwino panalibe abambo kunamizira mzere wamafuta……tikunenatu ntchito zooneka ndi maso…….mmmh, pano at the speed the kwacha is nosediving someone is still monitoring the shituashoni like the academic fredom saga! tiye nazoni…….running gaffment is serous business!….
Zopusa za chiani. Osati opusa ndinu akulu? Amai, you spoke lot’s of sense. Carry on!
Keep up madam JB!
This is a woman who always sounds better in rhetoric but always never walks the talk