Kaliati offers marriage counselling: ‘Be passionate and romantic’
Minister of Gender, Disability and Child Welfare Development, Patricia Kaliati, has slammed at men who like walking naked along beaches of Lake Malawi but are coy to undress themselves in the presence of their spouses in their bedrooms.

Kaliati said marriage is supposed to be passionate and romantic.
She was speaking at Ulongwe last Saturday on the sidelines of the launch of Improved Nutrition for Pregnant Women and Under-five Children project.
Kaliati said the fight against HIV and Aids can only be won if couples are open and faithful to each other where they enjoy the fruits of love immensely to stop cheating.
“Women should completely submit to their husbands and be open to each other in order to end promiscuity to fight the pandemic,” she said.
Kaliati said many men get married, expecting to have wonderful intimate relationships with their wives.
She said intimacy is an important part of marriage to avoid men or women seek outside their marriages to fulfil those needs.
Follow and Subscribe Nyasa TV :
Mumavutikilanji kumakwatira atsikana abwinobwino osangetengelatu mahulewo payambilila pomwe ndikumanga nawo banja. In marriages both a man and a woman have their own problems.
Akweni is exceptional
u should get some make up tips fast or else amuna anu apeza kena kokutha kuphoda bwino..shaaa nkhope ngati kapoli choncho…koma pillow nde amazionela kunyumbatu
Wezzie baulen it seems munakomana atabwali ndi ur hubby you need jesus and deliverance komaso it seems munaphana kaletu apa nanga nonse zibwenzi
Wezzie ukunama tikapanga chibwenzi ndi married lady we just have sex no material or financial support coz we know she just wants sex za finabcial support ndii responsility ya mwamunake zake izo
Zoona azibambo simunati tizikukanani manyumbamu because you dont treat us well.Kiss munasiya ,kuyamwa bele koma ngati mudule kuyiwala kuti limenelo ndi thupi.Ndiye ukapita kwina upeza zonse boo.Kiss smooth and gentle,sucking smooth and gentle ndiye utani?Ifenso timafuna chikondi.
Wezi bauleni you have ysled sense koma why cling to the man and refuse him sex osangomusiya bwanji mapeto ake he will screw all your sisters aunts and end up with ur mum
Kumeneku ndiye kudya kwa Akweni.Nkhani imeneyi amachita kukwezera timaso mwamba.Muli boo akweni.
Kaliat Stop Talkn Nonsese Here
Husbands love your wives as the Lord loves you and wives submit yourselves to your husbands Thanks Mrs Kaliati hope Mr Kaliati appreciates you.
I have attended one of her meetings. Kaliati usually digresses from the written script ndikuyamba zolaula zosagwirizana ndi occasion. I think she is sex crazy. At one time I could see the chiefs who were present looking down in embarrassment. Even if you gave her the ministry of foreign affairs, she would find a way of talking bedroom activities at a function. Hule!!!
A woman is submissive only to a husband who has been faithful to her. My story… I married young and was very submissive to my husband until he started messing up even the extent of bringing the hookers home when I am not around…since then he lost me into another man’s hands…yep!!!…he is out there in the cold!!! ntchito zamanja ake!!!
Iwe at 6,9,10. you should know that tikadziwa kuti wapeza chibwenzi ifenso timapeza chathu….tit for tat is a fair game…ndiye amakhala wabo!!! iwe nkuyiwaliratu kunyumba..nchifukwa timakana coz we know somebody is taking good care of us emotionally, physically and financially.. Most men do not take care of themselves…kusasamba..A woman naturally is attracted to a man who meet her needs…some men take advantage of their wives by not providing the basic necessities iwowo ndalama zawo zibwenzi, mowa and azibale awo leaving the wife taking care of the basic needs. If this happens believe you me it’s a turn off for most women. Even a well paid women would like to be pampered by her man ..in turn she will pamper him in the bedroom…ndangodutsamo!!!!
Mhh!!
A Malawi amakhulupilira kukhala ndi zibwenzi za zmbiri,abambo kapena amayi.akafika pa nyumba amangogona ngati chinkhuni chifukwa choti adya kale koyenda.
Tafunsani anthu a separation kapena devorce,akuuzani kuti sakufuna kubweleranan ndi wachikondi wawo chifukwa anazolowera kudya kanyenya kapena (takeaway)chifukwa cha chimasomaso.kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk isaaaaaaaa!koma edzi ilipo basi.aliyense atoyendera payerepayere kwanu maliro kwathu maliro
Bola zimenezi akweni mukunveka osati zijazi ife zimativuta kukomenterapo timaopa zikwanje zaachinyamata anu aja mumati macadete aja
Mayi Kaliati ungayende maliseche zoona nyumba zosunga achibale 100 pamalawi?Akweni mukufuna kupanga divert nkhani ya 599 billion.Romance imakoma zinthu zili malo mwake.Umphawi uli thoo.Aja amayenda maliseche kunyanja aja ndi amene anavuta ndi cashgate pakati paja.
Moni kaliati
Please help me with phone number ya Kaliati Mwina nkuonako za chilendo. I think she can perform
hule amanyekhula sizinaoneke. ndiye tisamathawe pa nyumba
uuumm,aaahh
kaliati tsopano
But it is a good advise from the minister,a husband and wife needs total submission to each other in the house, it is safe to do so, kunja kunaipa. It helps alot.
akazi ngati mrs kaliat ndi ofunikira kwambiri kuno ku malawi
Mukunena zoona akweni.pano ndatha mwezi kuchita ngati chaka osaopa.Azimayiwa amangoti atopa nthawi zonse.Muwayankhule amenewo.
Iyeyo Banja Lake Lili Romantic? Xachamba Bas Akagwere Uko
I would like to congratulate Patricia Kaliati for this insightful thinking. Most men end up in extra marital relationships because some women will often not talk or welcome their husbands in the home because they are broke. These are primitive women who will only smile at their husbands because they have bought them a gift or given them money. But lets face it, in Malawi, if you have not been ‘lucky’ to be a cash gater, where can you find the money to please your wife every day?
Kaya kkkkkkkkk mwina akunyumba kwao amateloso kkkkkkkk
Ndipo nso kuziziraku azikazathu akufunda ma blanket awo amunaso awo ndiye muziti muli pa banja kunamizanatu uku fundani limodzi muthese mphepo
Azimai mumanyumbamu akukana sex too much mapato ake bdi makofi ndikucheka manja kenako muziti gender based violence zausiru
Democracy tiuze zambiri
A minister bwanji? Ntchito ya marriage counselors imeneyo.
Koma nduna izi
Kaliata akunena zoona amuna ambiri amatha several months without sex chifukwa azikazi awo amawakana akuti atopa sakufuna etc mapeto ake mwanuna amapanga chibwenzi kapena kugona ndiwa ntchito ngati ali wa boo kapena aziphwake ang’ono wao azikazieo ngati ali pakhomopo kaliati azibwera ku ma bridal shower akukwana pa mwambo
Kkkkkkkkklkkkkkkkk
Pachibwezi ndiye kunyekula osati pang’ono, akakwatila kumangokhala ngati chikuni ndwiii, ma mood kukwiya za zii mkati. Choncho mamuna asasake konyekula kena. Kaliati you are doing a very good job sensitizing people about a health marriage and intimacy.
auzeni,amalawi satha romance
Zoona azimayi akuyenela azinyekhula bwino kuchipinda. Osamangogona ngati njanji.
Mr. Kaliyati , mwamuna wa Patricia, anabereka mwana kwa wa ntchito wake. Ndiye kuti Patricia samatha