Email a copy of 'Karonga police blamed for illegal transportation of farm produce ' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Namate
Namate
9 years ago

I thought our economy liberised . Pple r justified to sell their farm produce outside malawi bcoz production cost is too high and admarc and lazy pple want to reap poor farmers by offering them a raw deal. Let govt push the price of maize to K10000.00 rather than K4000.00. This encourages slavery as some pple think that the peasant farmers should b used to grow maize on their behalf by offering them peanut prices without considering production cost which is currently beyond K6000.00 per bag of maize.

Benjamin Mnyenyembe
9 years ago

Nde Mumafuna Tizigulisa Pa Ntengo Wo Cheap Osapeza Phindu, Ngat Akufuna Atisegulire Mtsika Koti Tizikagulisako Than Tolking Shit Pomwe Kumalawi Mtsika Kulibe Mavenda Amangotibela Basi, Kaya Tivutika Tilibenazo Ntchito What Mattars Ndikupanga Ndalama Zambiri, Karonga Ndi Town Ya Business Sitimangopangapo Izi Tikufuna Ma Flofit Ambiri Not Just Doin Business, Ndipo Tinasiya Kalekale Kudalira Boma Timapanga Dzathu, Chimanga Chikatha Tizidya Kondowole Ndi Mpunga Mwanva.

njomba
njomba
9 years ago

wow! Which market is readily available for maize in malawi? The government policy is weak, must bring market 4 the local farmers, not the bullshit

Ndalema nanu
9 years ago

chimanga ndi chawo ndipo ali ndi ufulu ogulisa komwe akuziwa kuti atha kupezako phindu lochuluka. so don’t put the blame onto the police but put it on our poor markets.

KADONOSHA
KADONOSHA
9 years ago

MWABANTHU TIKUSUZIKA WANYINU.MWENELONDO ROAD BLOCK YIKUTIVWIRA YAYE.IKUJUPHITSA EXCEEDING MIN BUS NA K150 MA REFUGEE WAKUJUMPHA NA MA K2000 IMAGNE.NGOMA ZIKUJUMPHA PARA DRIVER WAPERE K500 .ISE WAPOLICE AWA KUNO TIKUWAKHUMBA YAYE BOMA LIMANYE UKO LINGAWAYIKA.NAKO KUCHILUMBA WANTHU WAKUDANDAULA GALIMOTO YA POLICE WAKUTHIRA MAFUTA WAKUPOKA KWA WANTHU WA BUSNESS ACB IGWIREPO NTCHITO.

Uchitsiru Sasekana
9 years ago

Let the poor people of karonga sell their maize they need money to pay school fees buy other necessities and settle utility bills just like any other person the good thing is that they are selling the maize on their own and when hunger strikes they should be able to deal with it since they cant listen to the authorities on the issue of illegal sell of maize Karonga residents will be the ones to perish not the government ,me ,you or any other person Its their maize let them do as they wish with their produce Njala ikafika adzavutika… Read more »

Vyachalo
Vyachalo
9 years ago

Inde boma siyichitapo kanthu chifukwa apolisi ndiwo akudzembetsa chimanga powaloleza kuti zidutse.

Paramount Chief Lundu
9 years ago

These are the Police officers responsible for aiding kuzembesa Chimanga. MARIAM ALAMSON, ENOCK LIVASON, CHIPITA, BANDEWANDE, SAPUWA, EMILY BANDEWANDE, JERE, CHIMATIRO……………. MUKAFUNA MAINA ENA, NDIKUUZANI

jumujum
jumujum
9 years ago

Kodi amalawi mukuzemetsa chimanga makagulitsa maiko akunja, komatu musayiwala kuti February ikubwera yobvuta chakudya. Ndinu amene m’malankhula zamwano kuti Boma sichitapo kanthu pankhani yanjala pamene inu chakudya mukugulitsa kwa anthu ena. Apolice amangeni anthu mukagwira akugulitsa chimangacho.

Read previous post:
Marauding Tigers wreck havoc in Lilongwe: Malawi TNM Super League

Barely 24 hours after looting Area 30, the marauding Azam Tigers from Blantyre were on the loose again on Sunday,...

Close