Email a copy of 'Malawi army soldier, 2 others convicted over Indian Hemp' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi army soldier, 2 others convicted over Indian Hemp' to a friend
Malawi cannot construct a new airport at Chileka or increase power generation capacity without borrowing funds therefore the recent announcement...
Ma soldier timayanera kulingalira kaaa kuti tizing’aima adani ndiye inu mukutilandaso eti oky chabwino zaveka zimenezo!!!!
Ka 100,000 ndi salare yake yamwezi watha ndiye stiffpernaty imeneyo?
100,000 stiff punishment?Anyway since court limayendera malamulo not personal interest but otherwise mhmmm! itdosent sound stiff
just ligalize sativa canabis mwina maluzi mkuchepa
Amene sanachimwepo stone these people.
Sindikuwonapo nkhani apa.Kodi nkhani ya chamba ndi mlandube mpaka pano?Za zii.
More fire soldiers
Town yavuta iyi asiyeni anzanu azithandize awo..amene muli ndi mitu ya paper’nu osayelekeza kusuta izi muthamanga muona haha
MORE FIRE ZOMERA ASIYENI.
Stiff punishment shd hv bn K10,000,000-00 or 20yrs in prison,our laws need reviewing to curb the growing illicit drug trade destroying our country.