Email a copy of 'Malawi Catholic MPs celebrate Ash Wednesday with mass' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Catholic MPs celebrate Ash Wednesday with mass' to a friend
Within three weeks from last Thursday, when the Marriage, Divorce & Family Relations Bill of 2015 was passed unanimously in...
Mukasowa chonena ndi bwino kungokhala. Mudzaona zosaona inu! Mungathe kumezedwa amoyo ndi nthaka yomwe mumapondayo chifukwa chonyoza Mayi wa Mulungu.
Thanks to God for everything. May God bless ECM, our MPS and the Chaplain, FR H. CHINKANDA.
leave catholic alone
pali chifukwa chonyozelana apa ALAH azikukhululukilani* Kuzolowela Za UBOKO HARAM BASI
Akatolika ife timachita zimenezitu nanga inu? Kukumbusidwa kuti tizafa ndithu pofunika kulapa. Kodi hezekia adatani? David adatani. Adalisike anthu omwe adapezeka pamapemphelo amenewa.
Gonani you are a fool. When Muslims were being butchered by Christians in Central African Republic it appears you were happy and yet remained quiet. Fool! If you were a true Christian who loves peace you should have condemned that too. Opembedza mafano. Maria patsogolo, Yehova ndi Yesu pambuyo. Yehova akakulangani. Kuchinda ma sistere ndiye ntchito yanu ma father akatolika.
Catholics mafano basi palibe chilipo apa
I miss fr chinkanda my lecture at kachebere major seminary. he is a genius.
Nkhani yotsangalasa kwambiri,pitilizani kukhalira limodzi posaona chipani akatolika ndi amodzi
Parliaments around the world need prayers like these now more than ever to ask the Lord to save our Christian brothers and sisters in Libya, Iraq, Syria, Iran who are ruthlessly being killed by foolish islamic bastards there.