Email a copy of 'Malawi federalism demo set for April 8 in Mzuzu' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi federalism demo set for April 8 in Mzuzu' to a friend
Mediators in the ownership wrangle of Lake Malawi have proposed a resource-sharing agreement between Malawi and Tanzania governments. The two...
Mitu yathan nzeru atumbukafe sitingalamulire dziko tiye tizingodya nawo
lf the endorcement of federalism is tantamount to developmental mushrooming. Then lets have. Let every region have equitable lion’s share from every donor aid fund triggered in. Let us hold this gagantuan issue from the horns in tranguility.
ngati school yinakukanikani ndibwino musakomente chifukwa mukungolemba koma simudziwa kuti chalembedwa apa ndi chani?
This federal u want wil divide us
kkkkkkkkkkkkkkk Atumbuka mumandiseketsa ngati mukulephera kuyendetsa league yampira ya ku north mungathe kuyendetsa dziko? u are just showing your incompetence. Mukukakamila federalism cholinga muzidya ndalama za anthu ochuluka apakati ndi kummwera? Osapanga dziko lanu bwanji? Majority rules zowona. Inu mmesa kuli decentralization bwanji osatukula nokha north yo popanga mapulani okukomerani? Kulinso constituency development fund mudikira APM adwire fosholo ndiye mudziwe kuti mukutukuka? ganizani bwino pamenepa.
Ndiwe opanda nzeru anthu anu kumwera timawasunga ndife mma farm ife ndife ophunzi tikuziwa zosatira zake
Guys,those of u who are pushing for federalism,where do u live?popeza mumakhala ku bt or Ll munamanga nyumba zanu zokongola kwa eni.ndie mukufuna munthu wakumwera akapange mphanje kwanuko?mwauponda tizilamulabe.
In democracy majority rules,,why having rotational presidency? Let pipo decide thru the ballot who the next leader shd b.
Having comments from dullards like Kondwani cannot make Malawi to advance.He doesn’t have idea what Federation means.He is just exposing himself to the Forum how dull he is.Sometimes don’t just comment for things that you have no knowledge of.Pano sipolembelapo chimangirizo cha chi Chichewa.Vuto la anzanthunu mumadana ndi sukulu kwabasi.Wakuchulukirani ndi Umbuli.Kuchititsa manyazi kwabasi.
MALAWI FULL OF HEADLESS CHICKEN COMMENTS
WE NEED TO GO BACK TO XOOL
TOGETHER WITH OUR LEADERS
MAY GOD HELP US ALL !!! AMEN
Central and south yatukuka ndi anthu anzigawozo okha inu mumakamanga kwa eni kuthawa thengo lanu bwanji? Inu mukuyembekezera wina akutukulireni kwanu????????????? mulibe ulesi pitanipitani kamangeni kwanuko munkafuna tauni? pitani kumzuzu mukakometse ngati blantyre nad LL.