Email a copy of 'Malawi men asked to take part in family planning' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi men asked to take part in family planning' to a friend
Malawi’s Standard Bank has announced the postponement of the Joy of Jazz concert until 2015, due to scheduling commitments of...
Kodi mai mungandipatse email address yanu kuti ndikuponyereni mau oti ndimakufunani? Osanama Bingu anali osankha akazi ngakhale anali wa jang’ala. Choonde mai nditumizireni.
Madam Carista, your are fit to be a First Lady not the current one – nkhope ya current First Lady imatikumbusa Ethiopia tu.
eeee mainu ndinu owoneka boooo,mukanakhala size yanga yoti mwendo wanga nkukwanamo ndikanati tikambilane,koma you are like my mum
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk! wamandazi anabera game ya mwini, simukuona kuti she lost vision penpake, anangoyamba kuyika malibwe paliponse kkkkkkkkkkkkkk! @ chemwali
Anati, tibalane,tichulukane ngati mchenga wa kunyanja, anatero mulungu pouza adamu ndi hava munda mwa eden muja.
Kalista ndi mkazi wokongola. Moti ineyo ndimafuna nditaonana naye pafupi. Amandiwaza.
Ineso amandiwaza aise.
When politicians become safe motherhood coordinators. Calista, don’t bring back the outdated ideals of “TBAs”. Those people had their job description changed.
Wayambanso Calister Mutharika kusokosera? Abale give us a break.
Seriously speaking, , of these people mentioned, who SERIOUSLY QUALIFIES to be the Presidential Advisor on safe motherhood? Dr Mwale, Dr Phoya, Chipungu or Callister? I need your vote…….
Callista go to hell,you stole millions of tax payers money in the name of safe motherhood ambassordorship as your salary when your Bingu was alive.It pains me todate.