ANTHU OPUSA INU MCHIMODZIMODZI KUNYOZA BAMBO AKO WINA ANKOMENTA AKUTI KUKHALA PRESIDENT KU MALAWI NKULIMBA MTIMA NDI ASASAMBA OMWE AMANGOKUTUKWANA ZOONA PRESIDENT ADZIYIMA PA NZERE KUDIKILA NDEGE MTSOGOLERI WATHU NDE ANTHU KUNJAKO AMATINYOZA BWANJI
Denny
8 years ago
If Britain, a donor nation to Malawi has it’s Prime Minister who takes commercial air transportation and still looks respectable in the eyes all other leaders and they have a health care where when Malawian government officials get sick they go to get medical attention simply because we can not maintain our hospitals to the liking of our government officials who are themselves the mis-managers of those donated funds meant to upgrade or equip our hospitals. Now this nation Malawi that miss manages such donor funds wants a presidential jet for its President???? Tell that in the eyes of the… Read more »
kusyeje
8 years ago
President amakhala vvip & pilot akamanyamuka amalengeza kumulandira president aboard ulemu okhaokha, zachitetezo akulu zimenezo palibe angaphe nyapapi. Ndege running costs afumu sipano parking yokha pa airport not less than Us$ 500. Nzeru ndi imeneyi kukwera commercial flight zomwe apanga ngakhale azingotinamiza kuti apezako ma investor koma osawaona mpaka kutuluka m’boma.
patricia kaliyati
8 years ago
Ameneyu adzikwera economy class kuti achepetse expenditure. He should work hard to deserve and earn a jet. Actually he says he is rich why cant he buy a personal jet because he has to sacrifice. Bushiri akugula yekha dzimenezo because he works hard, he deserves it and he earns it.
BigMan
8 years ago
Poor Malawians, as usual obsessed with jelousy and trivia.
Kamuzu Mbewe
8 years ago
Apa osadziwa ntchito ndi ma ADC ndi protocol officers. There are special protocols used when a VVIP is traveling on a public flight, providing it’s business class.
Which airport is this? ziliko kunyasa
Anthu akusowa chakudya ndege yachan zopusa
Totally bullshit!!
zonpusa agalu inueti